Email a copy of 'Nam owes Malawi Queens K1 million: Players want unpaid allowances settled' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Nam owes Malawi Queens K1 million: Players want unpaid allowances settled' to a friend
Mzuzu University (Mzuni) student Kwenji Tembo was Wednesday night attacker by his fellow student for allegedly being involved in the...
NAM zochititsa manyazi iwambiri K20 000 ndi chaninso R500 SA money ai zachisoni kwambiri maiko mwanzathumu amawapatsa ndalama zambiri or ataluza koma inu mwawapeza atsikana olimbikila ngati awa osayamika bwanji, atsikana awa akuyenela kukhala ndi njale yakeyakeA BMW, Audi, VW polo koma ia K20000 kanuko mukuganiza kangapindule chani pamiyoyo yao, kuno Ku SA anthu o mixer mato amalandila R200 pa tsiku almost K8000 x28 days how much does this guys earn a month
MWAONATU NANGA PALI MAU:mungakame bwanji mkaka pamene ng’ombe ilindinjala musayembekezele zabwino pamene simunazale zabwino: yambani mwadyesa ng’ombe kenako kamani
mkaka: ma QUEENS ATIIKAPA MAP PAZIKOLONSE
Nam iwonepo bwino pakulephera kupita kwama player ena or kusachita bwino, Maykhulidwe a Mary waya ndi o pasula chonde chonde!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!
Bvuto la a Malawi ndi kukonda ‘kupakula’ kapena ‘tiwamwere’
Malawi will never develop” unless we fix the leaking bucket, the main problem its Cash-gate.
cashgate of the sponsorship money. malawi sadzathekadi ndaona ine.
20 pin allowance??????????? now i understand mwai kumwenda snubbing of the queens!!!!!!!!!!, malawi sazatheka, kuchuka kupakula koma!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!
Malawi!