Email a copy of 'Nankhumwa et al must take the blame for DPP loss' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Nankhumwa et al must take the blame for DPP loss' to a friend
Calisto Kalinda and Zikhole Ngulube were on target as Mafco FC won 2-0 against Mzuni FC at the Chitowe Stadium...
Hahaha hahaha
Thank you informant for giving us that information which is an eye opener on what is happening in government.
hohohohohooooo muuzanaaa……………………………..Dpp ikufunika mapempemphero atali atali
Kuluza kwa DPP kwadza chifukwa chadyera la azitsogoleri ena. Kumtundako omwe amamunamiza president.
Mukapanda kukonza zimenezi 2019 don’t blame nankhumwa again alipo ena akuononga.
Phwaaaaa
No blame games here , was nankhumwa the only one anayendetsa chisankhochi.
Hahahahah
Paja ku DPP madana ndi anthu olimbikira plus kuthandiza.
Ku mayani DPP idawina ndipo Hon Nankhumwa takhala tikuwaona kuno.
Nankhumwa as director of elections in the party tried his best vuto Secretary general dyera.
Nankhumwa was director of elections in 2014 and DPP won , akavuwevuwe abwerawa akuononga chipani .
In ndirande kodi magetsi mazimitsa aja nde akjpwetekani kodi nankhumwa paja ndi nduna nyachani’
DPP suppoerts vomerezani don’t blame munthu apa masankho anakuvutani basi
Nankga olo tinene nankhumwa zisankho zisintha? ????