Email a copy of 'Nankhumwa takes ‘register-to-vote’  tour to Lhomwe belt: ‘Give Mutharika, DPP votes in 2019’' to a friend

* Required Field


Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...
newest oldest most voted
Notify of
Citizen MW
Guest
Citizen MW

DPP may continue to focus on the old illiterate people. You may cheat those people. Unfortunately for you apumbwa, the majority of voters next year are the young and literate people.
For once, can you ably tell your audience what you have achieved in last 4 years which has their lives, and then new things you will implement when voted back in power. Dont just say vote for this “ntchona”. Malawians are tired of this childish politics. We must seen to be loving our country and not continue to be greedy.

Ndikunyenyaninyenani Pumbwa Party
Guest

Mbava izi.

Kaitano
Guest
Kaitano

Koma abale wina ndithu ndikumakwela pa chulu mkumadzikuza kuti ndi olemera pakati pa anthu ake amenewo? Abale are we really serious kumanamiza anthu ngati amenewa kuti one day they will see themselves in the Country that will be looking like Europe? aaaa come on guys, basi ndithu Mimba zikuluzikuluzo mkukhala pamwamba pa Galimoto kuti muoneke patali kwa anthu ake amenewo? mwawasiyila chiyani pamene mumachoka? mmene akuonekelamo, ali ndichakudya mmimbamo amenewo? amasambira soap koma amenewo? zofunda alinazo? koma abale inu, moyo kuwawa bwanji?????? Zoona tikamati ndine Phungu ndipo ndidzasintha miyoyo yanu, what does it really mean? to make them walk from… Read more »

Tiyanjane
Guest
Tiyanjane

I am not DPP, but I do like the young man’s new way of delivering DPP messages. Kaya Mchacha ndi Grezelder akuphubzirapo kanthu kaya

pathfinder
Guest
pathfinder

just look at the crowd, i think this battle is between chilima and nankhumwa. chifukwa achikulire a peter akadzati achititsa msonkhano, chilima ayandama kwambiri. chilima size yake ndi nankhumwa osati peter, mwana chilima wachepa.

Mchacha the Terrorist
Guest
Mchacha the Terrorist

@ pathfinder By achikulire you mean the inept guy masquerading as president?. Nanunso koma inu a pathfinder you are simply a waste of space seriously. This is a guy who has simply failed this country and the last 4 or so years he has been trading as president of malawi has been by all measure and standards a wasted time for malawi. Ndiye paja umatukwana za mkati utukwane. China Chilichonse ungatchule Iwenso ulinacho Kapena mbale wako ali nacho. But one thing that I will always say is that malawi is a country in need of redemption becuase of DPP ‘s… Read more »

Zandiwawa
Guest
Zandiwawa

Anthu ali pa msonkhanowo akuwonetseratu kuti akuberedwa look at their faces and attire.Ena akusowa ndi ndalama zomwe zogulira chipeso kapena zometetsera.Malawi is in deep trouble

BOLINGO
Guest
BOLINGO

DPP is making us poor as the handclappers look so that we will be handclapping forever

Gembe
Guest
Gembe

Poverty written all over the faces of hand clappers.

Agenda Setting Theory
Guest
Agenda Setting Theory

I agree with you, these are the people politicians abuse and they have been like this for years and they will be for many years to come.