Email a copy of 'Neno magistrate under fire for corruption: One victim appeals case to High Court' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

12 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
KAPOLO NENO
KAPOLO NENO
6 years ago

Ngati ndindalama zakuchulukirani Amaliana ndithu mukanamathandizako athu akwanu. Osamawonjezera khani ngati mwantundu uwu. Ife tikuthokoza kuti mwati khaniyi ili ku high court ndipo tizavanso zotsatira chochokera ku high court koooo!!!. Ndikufuna ndikumasuleninso inu atolakhaninu kaya ndiwe Maliyanawe kuti ngongoleyo inali katapira ndipo anatenga si Mapepuyo koma Mayi Solofina Ngwenyama yemwe amkagwira ntchito kwa Nzungu wa ku Partners in health. Ndipo mzimayi ameneyu panopa ali ku Blantyre, khani yonseyi a court la Neno akuziwa. Kupusa kwa Maliana anamemeza aganyu kukalanda katundu wa Mapepu. Amagistratewo ngati mumawazonda pa khani zanu musaphatikizire ndi khani iyi. zikomo

Bright
Bright
6 years ago

OK

Gilbohna
Gilbohna
6 years ago

No comment

mbooga kamfumu
6 years ago

banja kutha ngatia akuthetsa chibwenzi akuti ampatse 70,000 koma anthu ena kuamatchaja ma million koma Dzowera

mbooga kamfumu
6 years ago

dzowera ndikhalidwe lake ndinaonera pa nkhani ya mwana wa vesikani yotamu Kulu enaake anamadya bwino okhwima pa Neno pompo

how
how
6 years ago

Ine ndinalipila ndalama mwinikhani atachosa khani Ku court

how
how
6 years ago
Reply to  how

Akuti tax as I don’t pay tax

chimwemwe
chimwemwe
6 years ago

Mmmm enanu you just want to turnish the image of this good man. Magistrate went to school and he knows his duty. Don’t disturb him. ACB in Apinata nso ku school amve from both sides of the story. Inu atolankhani bwanji simunafunse nkhani yi kwa magistrate kuti mumve zoona zambali yawo? Zama bodza izi mxiii

how
how
6 years ago
Reply to  chimwemwe

Akulu sinayambe mwakumana naye

Kabula nigga
Kabula nigga
6 years ago

Mr Dzowela you are a shame to law profession. are you not satisfied with what you get?
mmesa anthu inu mwakhala mukunyanyala vepi to have your pay gone upwards?

Ntchona
Ntchona
6 years ago

Our country has gone to the dogs not many government officials have work ethics. Introduce a compulsory work ethics subject from primary to university to deter people from stealing from the state. Corruption is a hibby in our country

Donda warrior
Donda warrior
6 years ago

Nkulu ameneyu akuwonjeza ziphuphu. I remember mulandu wa Namagonya officer wa ku Neno hospital anadya ndalama kuti chilungamo chikhote.

Read previous post:
MPICO says investigations follows restaurant fire at Centre House Arcade building;

MPICO Limited says it is investigating the cause of the fire accident that occurred at a restaurant at its Centre...

Close