Email a copy of 'Nepman does not claim owning hit song ‘Chilawe Changachi’ – Manager' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

10 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
Chimwemwe Jack
Chimwemwe Jack
8 years ago

Oh shame Black Nina!!!!

James Jmt
8 years ago

Nepman n munthu wankulu

levelheaded
8 years ago

Ufuna achite kukutenga Ku show kuti nawenso utchuke? Unatchuka kale poyimba ndi otchuka kale nepman and’nso ukuwonjezera kutchukako pamene ukulimbana nayepa. Ine kuyamba kudziwa kuti kuli oyimba dzinalake lakolo.

Zumayi Katongo
Zumayi Katongo
8 years ago

Musiye mwana wa mugetto. oziwa kupeka yekha

mapwevupwevu
mapwevupwevu
8 years ago

Chilawe! Chilawe changachi! Tachilawe chikondi changachi! Chokoma ngati chakumangochi!

Sibweni
8 years ago

Black Nina kkkkkkk chilawe changa!!!!!!! Ukayenda ndi mwana wayenda wekha!!!!! Nep Man ndidamuziwa kalekale Akumaimba kwa Kampa ku ntonjani! Watchuka kamba kakulimbikila kwake!!!!! Kp it up Nep Man,,,,,,,,,,

Aubrey
Aubrey
8 years ago

Nina ngati umatha kuyimba tulutsa yako album. Nepman ndi dolo I we ndi kape. Nyimbo ukunenayo timaveraso pa chorus basi zako za unigers zopanda pake. Wayamba liti kuyimba?

Chikutumbwe
Chikutumbwe
8 years ago

Black Nina, Collabo ndi Collabo imakhala yopanda mwini….ndipo if you search it using your name as a prefix kkkk Google won’t bring the song up, unless we use nepman as a prefix

lackison
lackison
8 years ago

Black Nina , how many songs do u hv? Osangotulutsa album bwanji tigule ngati tikufuna

ntha.....
ntha.....
8 years ago

Oimba achiYo.. paMalawi. Nepman please beef him amve kuwawa

Read previous post:
Namadingo releases another banger ‘Macheza’

Just when you thought you had worn out the repeat button with “Msati Mseke”, Blantyre gospel musician Patience Namadingo is...

Close