Email a copy of 'New twist over Chande: Nomads destined player accuses Bullets of contract forgery' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

47 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
KWEENI MPULOFETALE
KWEENI MPULOFETALE
8 years ago

Neba kapena kuti ‘first born wathu” usatimvetse mutu ife makolo ako, Chande unamulephera mutakambilana, ndiye ngati mwini wake chamukomera kugwira ntchito ndiife popeza tamvana, iwe ingovomeleza,zisakuvute konse ayi, apo biii uyaluka sizinaoneke, chifukwa yekha walankhula kuti contract yako ndiyo forger, moti nkosavuta kuti malamulo achite nawe.
Iyetu komwe kuli mtima wake walongosola kale bwino lomwe moti iwe ingovomereza baaaaasi !!! Ukumbuke ‘kulemekeza makolo ako, kuti masiku ako achuluke padziko’

Spoter
8 years ago

Asasewele kwachsks ndiwadyela

Maston Majawa
8 years ago

Chande Akupita Ku Wanders Basi

Anafi
8 years ago

chande asatifute ayi kumene kuli contract yake ndikumene asewele kupanda kutelo ndiye chaka chino asazewele chifukwa playeryo ndiwakuba sangasaine contract kwina pomwe contract yake kubullets isanathe ndiye iyeyo ndiozokoneza.komanso iyeyo asiziwa kuti kupeza ndalama sathamangila ayi.ndilunzo alinalolo ndizotheka kuchita bwino sogolomo koma osati athamangile ayi ndizoona kuti chande ndiwabwino koma akamachi zophupuluma zitha kumuonegela zogolo lake

ibrahim bullah
8 years ago

nebah jafali asakupusise takhalanae tikumudziwa uyu..wakudyela ndalama sanafune kukuuza chilungamo

thokoc
thokoc
8 years ago

FAM SHOULD COME OUT CLEAN ON THIS ONE OTHERWISE IT HAS VIOLTED ITS OWN CONSTITUTION BY ALLOWING A CLUB TO USE UNREGISTERED PLAYER. ITS TIME FOR ACB TO INVETIGATE THIS ISSUE. LET HEADS ROLL NOW. THE PLAYER AS WELL SHOULD FACE THE LAW. FAM EXCUTIVE SHOULD AS WELL GO NOW NOT TOMORROW. WHO IS FOOLING WHO. AMENE ZIRI MMANJAYO GAME YAGONA

spectator
spectator
8 years ago

Osamusiya player spite komwe akufuna bwanji. Miyendotu ndiyake

WILLARD MUBVUMBI
WILLARD MUBVUMBI
8 years ago

If it is proved that Bullets forged the papers, a deterrent measure should be taken. Its a serious case. The club can be banned for a certain period. It will be a warning to would be perpetrators. Players are not slaves and they have the rights.

Justice Nyasulu
Justice Nyasulu
8 years ago

foseki manoma manaoma ndiyr kuti chani muti chande atuluse yake cotrakit osayitulusa bwanji mwayambila muja? Chande akuthawa ku bb simagawa maswit bullets ngati suukuiwa neba

beje
beje
8 years ago

kkkkkk sanafike pofuna 3 million ngat akufuna kupeza team ina atha kupita.munalepherana mitengo ndiye mwana anayamba kusaka omwe angamupase 3 million.lero mwaona zayamba kutheka mwati ayi imeneyi ndi njiru anzanga a bullets.lero ndiye mwaona a harod fote ndi msungama kuti ndiofunika poti palowa njoka?

Read previous post:
Kanda Bongo Man headlines Malawi Awards UK: Piksy, ‘Tsika’ tune maker, Sonye in the mix

With his easy rolling vocals and upbeat, cheerful and rhythmic tracks, he is one of the key figures of African...

Close