Email a copy of 'NICO boss slapped for flirting with Doctor’s wife' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'NICO boss slapped for flirting with Doctor’s wife' to a friend
There has been a steady rise in the number of people visiting www.tiwerenge.com, a website whose purpose is to expose...
Eric nkukhala kwake wathetsa mabanja ambiri like Liness Liabubas(mrs Maburekesi)
Koma lake silitha.
Mmmm, azibambo muzifunsa history ya mzimayi musanamukwatire. Wilma timamdziwa ndi mmene alili kuyambira kale kale, olo ku college anayamba wakhalako ndi mwana and came back to finish school later. Inu kapena bambo Chalulu munkaona ngati inuyo nde ndinu dolo loti likhoza kumufatsitsa Wilma? Leave her alone. Its her right. Nkhani imeneyi kuti akutengereni ku court mukaluza and muluzanso ntchito yanu if you are a government doctor. Musiyeni mzimayi bola ngati amakulolezani game, kwinako bwana Chapola adzikachitanso pan’gono.
Chima akamenyenso Sumbuleta….wapukusa kwambiri.
Tandipeza ndikupatse chambu, akadzalowamoso adzatupa machende mpaka kuphulika,
Poti anapangapo kale kambilimbili im calling al-Qaeda there is a job for them, they should sort out this nico boss and
Can someone be brave kuti naye akamuzondose mkazi wa chapola akamupolamike mxiii
Kuchapa mfuti bwana chapola.azanama hule wa doctor, mamuna MDI mwana
Mamuna akamanyenga ndiye its OK? There is nothing wrong with mkazi wokwatiwa kukhala ndi chibwenzi. Azimayi have tolerated a lot. It’s time men start understanding that women have the right to be promiscuous. A man who wants a clean marriage should not be promiscuous. The wife will follow suit.
Kodi flirting ndikunyengana?Flirting is feel good basi.Mukananena kuti anawapeza mu room kapena.Palibe nkhani apa.Men you cheat and you expect us women to just sit phwii kumakudikirani kuti mukatopetsana mutipeza?Time up!!!!!!!!!
Ndiponso inu azibambo a Malawi simudziwa kukonda mumangodziwa zinazo basi shupiti.
It is our time to feel good.
AGALU INU KUKONDA KUTUKULA MALIPHYATA MUKAONA NJOLE YANZANU.
Mmmm, azibambo muzifunsa history ya mzimayi musanamukwatire. Wilma timamdziwa ndi mmene alili kuyambira kale kale, olo ku college anayamba wakhalako ndi mwana and came back to finish school later. Inu kapena bambo Chalulu munkaona ngati inuyo nde ndinu dolo loti likhoza kumufatsitsa Wilma? Leave her alone. Its her right. Nkhani imeneyi kuti akutengereni ku court mukaluza and muluzanso ntchito yanu if you are a government doctor. Musiyeni mzimayi bola ngati amakulolezani game, kwinako bwana Chapola adzikachitanso pan’gono.
A dokotala poti mulikuchipatala kale mudziyezetse kachilombo.
Mkaziyu wathana nanu basi. Muli muwebu?
His wife anavomereza basi kuti Eric yo ndiwonyenga and ndimmene alili nde its either she leaves or stays and accepts him as he is…….bola kukhala mrs basi