Email a copy of 'Njawala set for Blantyre Kabula comeback' to a friend
Loading ...
Minister of Information and Communication Technology (ICT), Henry Mussa, has taken on the public broadcaster, Malawi Broadcasting Corporation (MBC), encouraging it...
Zoona ku UTM kwakoko akukanika kukupasa nsalu yoti uziyala pakaTebulo kako konyansa ko???
Gerald, Lunzu yatopa ni Hon Minsiter Chazama. Chimpangireni unduna ikuyelekewa kwake. More fire Gerald
Mkango, Mango, PA Container, EMU1, Summer Field, Vicky Half London, Hard Rock, Two Sisters, White Village, Alinafe, End of Rusternburg tonse pambuyo pa Gerald an SKC
Which developments? Mwangosowa ntchito mukufuna ife tikulembeni.
My fellow software engineer, wish you well
That table is not even made by a graduate from TCC. What and Where did you leave behind? Bodza akili Loma musataye nthawi yanu. Just continue what you had been doing after your loss.
Ana Amuna awa. Mr Action Man. Kulemera sikuti ndi chitukuko ayi koma passion for the people. From mbayani to Md’ala ntchito zanu zimaoneka. Everyone wants you back . And Gerald the constituency can’t wait to vote! Nonse awiri mwawina kale. Mulibe kudzikonda anyamata inu. You mix . M’memo timadya limodzi. Viva Felix. Viva Gerald!
Awa anzawo kwathu kuno akuchita kuneneratu kuti ife ndiye sitingawine koma tingofuna kumukawa Arafat Hamdan yo.
@Gremo
Ukakhala kuti umadana ndi munthu winawake popanda chifukwa chenicheni cha mzeru umayankhula ngati mmene mwa lembera inu mu