Email a copy of 'Njobvuyalema elected SADC parliamentary vice chair' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

30 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
zanimuone
zanimuone
9 years ago

AChakwera muli ndi anthu mnyumba yamalamulo, anjovu alipompo, komaso akamuna awa akukasungu achipatala chaCANCER aja. Mpaka pano boma lilibe mau, yewo CHAKWERA and team.

sauzande
sauzande
9 years ago

Ife timafuna anakavotela a patricia kainga nangozo a ku zomba central osati a. njovu tiyese amayinso. Poti zachitika we will suport him ife a pp

TSAMBALIKAGWA
9 years ago

Good boy Hon Njobvuyalema, Wishing you all the best, continue to be loyal to MCP & its Leadership, Bravol Mcp! Bravo Lilongwe mapuyu south MP! Kumeneko ndiye kubwera wolemekezeka!

Anonymous
Anonymous
9 years ago

iwe namba 21 ukuti njobvu simuthu wamba koma mndani? kumangokweza zilizonse mumtengo, iweyonso simuthu wamba inenso simunthu wamba

Concerned citizen
9 years ago

Congratulations. You have made us proud.

Please ensure knowledge transfer to our parliament.

Chabwera Phiri
Chabwera Phiri
9 years ago

Congratulations Honorable Njobvu.

phunda
phunda
9 years ago

Congrants

Momo sam
9 years ago

Malawians learn to say ‘CONGLATULATIONS’and i thnk he deserve the post,am not an MCP fan but most of their MPs are amazing look for example hon.lunguzi,dr.elias chakwera,njobvu,jumbe,chankhwatha,sam kawale,they are amazing in the assembry,jelasi dauni ma man.

Munthu wa Mulungu
Munthu wa Mulungu
9 years ago

Chala cha Mulungu chikakuloza sizisowa. Congrants, Bwana.

Bwalero
Bwalero
9 years ago

Njubvu simunthuwamba

Read previous post:
Court defers Mulli’s stay order: Fights MSB over K3.2 bln loan

The Supreme Court of Appeal on Monday deferred to a later date the application by Mulli Brothers Limited (MBL) to extend the...

Close