Email a copy of 'No December pay for anti-graft striking staff, Malawi govt says' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

76 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
rif
rif
9 years ago

ACB tsopano! Eh, koma a Malawi ali ana ako ungangoti, nkadadziwa sinkadabereka

thebsom
thebsom
9 years ago

Mu sova guys ine za strick zanuzo ndiye ayi ndaonapo anthu akufa kamba ka ma strick ngati amenewo ine ayi !!!!!!!!!!!!!!!!!!

zako izo
zako izo
9 years ago

cum 2gethr and resolve the differences amicably,,mukalepherana ndikukwapulani

christian
christian
9 years ago

The issue is simple,we work to get payed,so if we don’t work how can they get paid.

Phodogoma
Phodogoma
9 years ago

Aku ACB mumangomva strike eti. Inu anthu a contract mungachite strike bwanji? Boma litakhala pansi ndi maloya awo ndikuunikira bwino nkhaniyi atha kukuchosani nonse popanda ma benefiti. Koma boma silimaziwa ma elements a milandu ayi. Inuyo a ACB ndinu olakwa zedi. Zinthuzi mwazitengera ndale basi. Kodi ndimayesa mudasaina kontalikiti ya zaka ziwiri kapena zitatu mukulandila salary imene idali mu apointment form yanu? Ndipo mudavomera kulembedwa ntchoto ndi salary imeneyo.Ndimayesa mumachita bargain for good salary during contract renewal. Tsopano umbuli bwanji? Inetu ndagwira ntchito ya contract. Ngati contract package yachepa umakaniratu contarct. Kotero kuti kuonjezeradwa malipiro uli pakontract ndi mwa chabe.… Read more »

Onawaka Gondwe
9 years ago

That’s a good point. and legalize same sex marriages tikwatile ife

Mzungumaso
9 years ago

Masiku akumapeto,
What we are supposed each other is to read the Bible and see what it says about the great controvency. Later each Malawian should count of his doing.
Thank you

Kondwani
Kondwani
9 years ago

ationongera dziko anthuwa.

Hoitty
Hoitty
9 years ago

Musapatse za December anthu a dyera awa. Inu a ACB ngati simukufuna harmonisation siyani kumeneko zaloweni m’boma. Ndipo strike ikatha ena osapangira renew ma contract kumeneko.

Osward Kayange
9 years ago

Kaya Amalawi

Read previous post:
Malawi inflation at 23.7 percent year-on-year

Malawi's consumer inflation edged up to 23.7 percent year-on-year in November, from 23.3 percent in October, the statistics office said...

Close