Email a copy of 'No repeat of July 20 killings, MCP Diaspora warns' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'No repeat of July 20 killings, MCP Diaspora warns' to a friend
Shortage of facilities in Malawi’s hospitals continues to rear its ugly head at Chirumba rural health centre in Karonga where male...
Za ziii…. get married and enjoy American burger.
Thanks Chitembeya for the concern but come home and make impact. You can not be making noise while in the UK or US. With or without you we can make the noise and change Muntharika. Peter was also like you leaving in the US. The difference is only that he was teaching at the University while you are taking care of azigogo akwa Zunguko.
Koma MCP yathadi mpaka Lucy Chitembeya. Is this the same Lucy from the Kasungu Mayard Chitembeya? I hope not. If it’s real her then MCP yasowa anthu ku Mericako. Hahahahaha@koma yes.
Diaspora ndiye ndaniso. Why don’t you just come back home musiye ma shift anuwo. Za zii.
Macadet umbuli! President APM was diaspora for over 40 years before coming here.
Abale kongilesi sinasinthe. Akudela nkhawa ndi zomwe zinachitika pa July 20 koma chipani chakuphachi sichikudera nkhawa ndi zomwe zinachitika pa 18 May 1983 pamene kongilesi inapha nduna zitatu ndi phungu m’modzi ku Mwanza. According to Chitembeya, she would not mind a repeat of MCP brutality. Shame on you madam for endorsing MCP brutality.
Amene ndi a ngwiro ndipo sanaphepo munthu wayenera kukhala ndi nkhawa…………… ndipo beasts, kunena kwa Callista, don’t care and can kill some omre. Komanso zitsiru, ntchito zao ndikutsatira zinthu mwa umbuli…………….!! Kodi a Dausi, a Ntaba, a Henry Musa etc amakuuzani kuti mu MCP yatsopanoyi alipo amene anali ndi udindo pamene MCP yao imapha anthu…………………… ngati alipo dzina lake ndi ndani? Zoona alipo pakali pano a DPP amene samadziwa zomwe anthu amene pano ali mu DPP amachita pamene anali mu MCP………………………… Ndale zanu ndi zonunkha, ndipo mulibe manyazi………..!! Sadly Malawians are now aware as regards which party the beasts belong… Read more »
A Chitembeya, what has the international community have to do with us? What did they do with the victims of 20 July 2011? What is the so called international community doing to prevent trouble in many other parts of the world. That is nonsense. Simungaopseze ndi mawu amenewo, ingobweraniko mudzakumane ndi tear gas inuyo. Adzakufukizani international community yanuyo ilipo, ikumva, ikuwona. Don’t put other people’s children in danger inu mutathawa
There is no such as thing as DPP government. There is only one government and that is Malawi government which will always be whether DPP is there or not, so it is better to say DPP administration or Mutharika administration. It makes me angry when people say DPP, PP, MCP, UDF government.
Inunso ndiye kayatu! Its DPP led government. Dont you know its the party leadership that makes government leadership? All cabinet is DPP leadership for example