Email a copy of 'No UDF candidate in Zomba Chisi Constituency by- election' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

12 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
H.CHITUVI
8 years ago

Chipani chotsutsa kulowa ku chipani cholamula chimadziwa kuti zake siziri bwino zathu zinada chilipo koma kutsanzika mwachiukulu tikufuna kuthandiza boma.Chiyambi chake ndi chomwechi mudzaonanso pa GE2019 madela ambiri sadzaimitsa aphungu.Chidayamba ndi Muluzi Snr.chidzathela ndi Muluzi Jnr.anayamba kuchizula nthenga ndi Muthalika elder bro amaliza kuchiduladula ndikuchikazinga ndi Muthalika yng bro.

Tonde
Tonde
8 years ago

Kkkkkkkk muyezo umene muluzi anayezera aford today wafika ku udf

apap
8 years ago

zabwino zonse Asma. udf idatha banz akudyayo ikatha azayambapo makan

bav
bav
8 years ago

Mathanyula ndi amene ali ndi njila yommalizila atu ndi kachipani ka bambo wake

Juma Mike
Juma Mike
8 years ago

Inu simukudziwa kuti Yudiefu inatha?Mufuseni atupere kuti agenda for change ili pati nanga malume ake a G chapola ali kuti?Chipani cha Fuka ndi MCP zinazi ndi za season nga fodya

ibrahim makwati
ibrahim makwati
8 years ago

I wonder where are u going with my UDF kapena mau akulu amakoma akagonela KUTHA NGATI MAKATANI

ibrahim makwati
ibrahim makwati
8 years ago

I wonder how long i can keep myUDF like this bad divolpoment

Victim of misery
8 years ago

Udf is dead and gone kkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkk

Kandapako
Kandapako
8 years ago

Ayi kuchimalizadi mwana chuma chobambo kkkkkkkkk

patricia kaliyati
patricia kaliyati
8 years ago

IT IS FINISHED?

Read previous post:
K2m student’s examination fees stolen at Thyolo Secondary School

Robbers armed with panga knives on Monday morning stole K2 million worth of school fees at Thyolo Secondary School, Police...

Close