Email a copy of 'Nomads book Carlsberg Cup final berth against BB: Malawi battle of battles' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

22 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
Mpinganjira wa manoma
Mpinganjira wa manoma
8 years ago

the wise people’s choice. well done my team

Bambo a Temaco
Bambo a Temaco
8 years ago

Wanderers ndiye yaziwilatu kuti ikazisiya pa 29

ntex
ntex
8 years ago

Timafuna iwe kumene uwine kuti BB izadutse moyera nyelere yatola Jokala watiyiwala nthawi yomweyi ndikukubechera wanoma na pa BB siuzapezapo chimwemwe ukhumudwanso pa 29 pano sindikukayika konse Maule ndi more mphwanga aliponso wina

Easter
Easter
8 years ago

Njaliwa was my man of the match not Chipuwa

Hardson
8 years ago

Kodi guyz mukuliralira eeee iyayi Moyale inayenda kwambiri game plan mulibe eti. Palitu ndi mipira yake yomati tikasewerere ku mpoto kummwera ndi pakati. Do you mean you have faile to pregress simply becoz you played away? Tanenani! Ngati ndi choncho mutuluke mmipikisano chifukwa simuzitha. Mudzangobwera pa 29 ku Civo mudzaone ndikuphunzira zimene matimu a ku Blantyre amachita akafuna kutenga chikho curtsy of Big Bullets. Nanunso a wonderers, kuwina mu mpikisano waukuru ngati uwu sitimawina ndi 1 yokha ai, ndi zimene mukwapatsa zolankhula a Moyale. Mukuona Silver Strikers ili ndi mau aliwonse, akudziwa kuti anagonja bwino, 3-0 sangakhalenso ndi mau. Any… Read more »

Hardson
8 years ago

Bola pamenepo! Bullets 3-0 Silver strikers. Wonderers 1-0 Moyale = Bullets 2-0 Wonderers come 29th August 2015 @ Civo Stadium.

Shocker
Shocker
8 years ago

FAM/Carlseberg + Noma 1 – 0 Moyale Congrats to FAM / Carlseberg Malawi Limited and Beforward Wanderers for winning against the tired and frustrated Moyale Barracks F.C. You staged the competition to make it suit your wishes and desires. You never considered fairness and competition in the game of football to guide your decision making. You made Moyale travel through out the competition in order to frustrate them. No team can be happy to play all its games in a competition away from home unless its home ground is banned. If all you want is Bullets or Wanderers to win… Read more »

isaac kudala
isaac kudala
8 years ago

cogrants neba, koma ukunzekere pa 29.maule mo fire

Emmanuel Kabaghe
Emmanuel Kabaghe
8 years ago

zilibwino.ife ndi manyex & wi shall remain like zat.

Duncan kapunda
Duncan kapunda
8 years ago

Am sure nyerere mwazipachika pamtengo waminga

Read previous post:
DPP warns against voting for opposition in Mzuzu by-elections

The Democratic Progressive Party(DPP) has warned registered voters in the forth coming Mzuzu city’s Chibanja ward by-elections that they risk...

Close