Email a copy of 'Nomads lose to Civo, title bid meltdown: Malawi TNM Super League' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Nomads lose to Civo, title bid meltdown: Malawi TNM Super League' to a friend
Malawian President Peter Mutharika Sunday returned home from China where he among other things attended the World Economic Forum (WEF)...
Neba anazolowera zogwera basi,more fire the people’s team.
i will not stop supporting my B4wd no matter what..
Munthu mmodzi kukomenta kambirimbiri bwanji osangoleka kkkk walilanayoooo Civo…….yakuyambitsa misala tsopano udzalira kwambiri.Dikira mudani wako Silver Strikers akubwera kudzakuthira nkhondo iweeeee.Maule ndibomaaaaa 2015 woooeeeeee.
MUONA TIPHA MATEAM
Fainal ya carsberg akuti imenyedwanso ref adakondera noma.
Kodi ma teamuwa tingokwagwera ndiye tikadatenga carsberg.
Ife timaliza team pa ma fainals.
. Noma oyeeee!
Kodi paja intercity adatenga ndi abb nanga bwanji aku samaluza.
Paja noma chaka chino siyidatenge chikho. Nanga bwanji akuti adatenga carsbage.