Email a copy of 'Nomads sign two players: Tambe and Namwera in for undisclosed deals' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Nomads sign two players: Tambe and Namwera in for undisclosed deals' to a friend
Higher Education Students’ Loans and Grants Board has approved additional 373 needy students to get loans. It means, a total...
SANASEGURE KWA INUYO AGANYU
Paja ndi inu player aliyense mukumane naye pamseu bwela kuno,muzingowaunjika
Mwayambilanso zomwezija zomangosaina maplayer ambirimbiri kumasowa nawo chochita koma team imeneyi sizatheka hahahaha. Nyasa bullets ndi moto!!!
Zoooona nyerere tili limodzi
Nyerere Moto
Kodi a bullets vuto lanu ndi chani? Article iliyonse ya noma you are the first ones to comment. Ngati zakunyasani mukatunge madzi onse mu lake malawi muthirire mbeu zikuumazi .
NYASA BULLETS FANS INCLUDING EXACUTIVE PLEASE HELP BAULENI MASAMBELO FORMER BULLETS PLAYER WHO IS FIGHTING FOR HIS LIFE IN CHINSAPO,PHONE CHANCY GONDWE HE IS AWARE OF HIS PLOBLEM
The transfer Window is not open how come you are signing players?
How many quality players did you buy last season? if its 5 then should be 6. But what did you achieved at the end? One trophy and finishing at number four in the league. What about your neighbors? Without new signing but returning the title and displaying good football. Which means there is a lot to consider. So apart from the Tambe’s, organize your family. Its just an advise you can take it or not, accept or criticize.
Ndangomvetsedwa kuti NEBA ( Bullets ) akupita kukaona odwaka Ku Zomba pa 13
Chonde amene muli ndi achibale kuchipatala cha Zomba adziwitseni kuti mafoni adzakhale polimba pa tsikuli kapena akasungise Ku police imene Ali nayo pafupi
Tigwirane manja pothetsa umbanda ndi umbava Ku malawi????