Email a copy of 'Nothing wrong with Nyasa Bullets deal: FIFA ok with tobacco company sponsorship to Malawi champions' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Nothing wrong with Nyasa Bullets deal: FIFA ok with tobacco company sponsorship to Malawi champions' to a friend
Malawian new music talent, singer and songwriter Sharon Tembo is releasing her debut single titled ‘Running’ which was recorded at...
Amalawi nsanje sadzasiya,kupanga zabwino ena kuziipitsanso,palibe vuto apa!or ikhale Fodya Big Bullets sibolani Cashiyo basi.
Nsanje siyabwino mawa udzakhala uli iwe neba
Thumbs up to Nyasa Manufacturing Company for taking on board our beloved BB, a word of caution to BB management, chonde kuba ayi ndalama ndi za osewera amene mavutika, timuyi ndi aife anthu inu tinangokupatsani mwayi wotsogolera mmalo moti tonse singatsogolere timu nthawi imodzi. I suggest may be Nyasa should also bring in their Finance people to look into finance issues for accountability purposes.
But Iam against those enemies who are not happy about BB getting sponsorship a malawi tiyeni tizikondana kusiyana matimu okonda sichifukwa kuti muzilemba zoyenera za timu ya anzanu ayi.
Typical of Malawian people PULL ME DOWN SYNDROME bola zanga zikuyenda we will never move forward ndi nsanje ,wake up !!!!
The future of NMC is uncertain? Ok what about that of second hand cars dealer which some countries have banned for pollution, do we have a future at the reserve bank continuing sponsoring a team with the economy in its current state. Tapezani zonena zina….
wanyerere olo ukwiye ndi ka sponsorship kako ka b forwad
kammanjako
mkhuku yanjilu siiswa madzila,wanyerere ukuenera kuvomereza kut Bb nditeam yolemera muno mmalawi .
Undwa zako izo mwana
Mapale mutha kusankha limodzi mwamaina awa for your team
Fodya bullets
or
Tobacco Bullets
or
Nyasaland Bullets
or
Khanundu Bullets
or
Chain Smokers Bullets
More fire mawule waza waza