E-Mail 'Nsanje registers 3000 primary school dropouts' To A Friend

Email a copy of 'Nsanje registers 3000 primary school dropouts' to a friend

* Required Field


Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...
Please share this Article if you like Email This Post Email This Post
  Subscribe  
newest oldest most voted
Notify of
DaDa
Guest

Federal system ikuchedwa tisamamve nawo nkhani zopusazi.mwana kuthawa ku xul ndekuti chani???

Richard Pankomera
Guest
Richard Pankomera

This is literally bad!! we need to introduce compulsory free primary education NOW and not later!!

....
Guest
....

Ali mtawuni muno ati “thandizeni bwana”.

bwampini
Guest

Nanunso a Nyasa mudziona nkhani zolemba ku nsanje kungakhale ophunzila… Bola kumpoto kkkkkk

kwa phelewera kwathu
Guest
kwa phelewera kwathu

Nawo alomwe ndi aSena ntchito kukoka makutu basi.school ndi imeneyo mukuyithawayo.koma mmawa lino mufuna kuti mukhale ma president muzizazunza anthu basi. Zonvetsa chisoni.mchifukwa chake boma langoganiza kuti likubeleni ndalama muonjezere kokagulira zida zo kokera makutu.

mabilinganya
Guest

This is a shit of a country!!! Forget about development

duduzi
Guest

Mwayamba kuyithawa nokhatu……..timakuwuzani kuti sukulu sachita kukakamiza ayi …KUYESERA KOTA koma AYI ndithu…..koma kulimbana ndi Mtumbuka ndi Northern Region yonse. Zitsiru kwambiri …..inu makamaka former Vice Chancellor wa UNIMA, Chapola ndi Bingu(do not rest in peace but burn to the bone in a hell of fire …for causing all the sufferings of the Northerners). Izitu zili ndi anthu kapena mtundu wake wa anthu olo chigawo………mwana Mpoto amakumana ndimakondishoni oposera pamenepa koma osayitaya sukulu ayi ndiponso no marriage arrangements kumene kuja. Nchifukwa chake mumaberekana ngati ngumbi – a BLM, PSI kuyesetsa kukuphunzitsani kulera koma ayi ndithu…..mapill olelera kukataya komanso nyama kunyama… Read more »

A chimwene mwalalata
Guest
A chimwene mwalalata

Akulu mwalalata inu. As a southern man, I am disappointed with these girls and especially their parents. I have been to the north, the motivation and material support that parents in the north give to their children is enviable. Too much poverty in Nsanje, occupied with what to feed their families tomorrow, what else could the parents of these children do? I am upset with our politicians, dam shire and any other river in Nsanje, get massive rice farming schemes going and start making a difference to these peoples lives. A sad lot of politicians we have: a sad lot… Read more »

womenslib
Guest
womenslib

You are a stupid and divisive fool. People in Nsanje have always been kept poor. These are the consequences of years and years of being ignored by the ruling governments and being treated as if they were foreigners in their own country. It’s idiots like you that will cause civil war in the country with your inhumane racist…yes racist and insensitive comments. If Malawi were to become federal your region will immediately be destroyed if it’s being run by idiots like you. We are a global village now. If you don’t understand what I’m saying by a global village take… Read more »

faines
Guest
faines

Zonsezi ndi a Tumbuka ozikonda. Kufuna kupanga distract from yopanda zimbudzi ija. Mwang’omboka

Nyaka
Guest
Nyaka

Choncho nanga mkutani? Kukupatsani Kota ayi ndithu. Sukulu mukuyithawabe.. Anthu osathandizika Inu. Mukatha Apo kutukwana atumbuka.. Mxi!