Email a copy of 'Nurses stage strike at Mwanza district hospital to demand transfer of DHO: ‘We are working as slaves’' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

7 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
MKUPHWASIKA
MKUPHWASIKA
7 years ago

Bola kumeneko less than 40?
Kuno tiliko less than 9 koma ntchito imakhalako osati masewera.
Dziwani lero kuti tidalumbulaa kugwira ntchito ku chipatala paja eti?
Kugwira ntchito ndi ukapolo mwanva anyamata ndi asungwana? umene aliyese tikhoza kumutcha kapolo koma ntchito zosiyana siyana.

M\'banga
M\'banga
7 years ago

Piringu is just boring, the kind of his administration UNCIVILISED I cant believe he was still DHO up to date, tinamuthamangitsa ku Dowa just in 2 months. Anzathu a ku Mwanza ayi ndinu opirira zedi

Fikisa
Fikisa
7 years ago

Iwe Alfred Minjo
I guess you are thinking retrogressively. Is it bad to upgrade from a med assist to a CO? Further ukuti mzake odzimva aliku chsu iwe amakulesa kudzinva ndani……get a life dude!!!

Alfred Minjo
Alfred Minjo
7 years ago

Mkulu ameneyu anafikapodi ngati kuti ndi dokotala weniweni. Koma zooona ngwa mwanodi. A medical assistant up graded to a Clinical Officer, koma iiiiiii. Nzake naye odzimvanso aliku Lilongwe ku CHSU.

Fikisa
Fikisa
7 years ago
Reply to  Alfred Minjo

Ukuganizila katumba ase…..

maluza
maluza
7 years ago
Reply to  Alfred Minjo

ndiwe ofoila zedi,you think being a medical Doctor is equal to being a good manager???..ma Dr ambiliwa ndie mbolanso bola ma medical Assistant omweo..apart from piringuyo

The Patriot
The Patriot
7 years ago
Reply to  maluza

Kapengeni sukulu madala, kudana ndi anthu ophunzirà sikupindulirani! Dr simasewela, asakufuna asiye!

Read previous post:
Zonda, Sulumba missing on Malawi squad for Cosafa Cup tournament 

Defender Pilirani Zonda and forward Muhammad Sulumba are missing on the list of Malawi's Flames squad published on COSAFA website...

Close