Email a copy of 'Nyamilandu welcomes Ahmed era at CAF: FA Malawi presdent says ‘change is good’ for African football' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Nyamilandu welcomes Ahmed era at CAF: FA Malawi presdent says ‘change is good’ for African football' to a friend
The Ministry of Gender, Children, Disability and Social Welfare and human rights activist Habiba Osman have condemned the parading of a naked woman...
Wenger achoke!!! Walter achokeeeee pakali pano!
Walter Nyamilandu,Rose Chinunda,George Jana ndi ena nonse amene mwakhalitsa we need change tione zina.
kkkk Nyamilandu mulibe manyazi eti payankhula zimanezi??? Nanga inuyo bwa?????
Nyamilandu, si ufumu woti mpaka wina asiye nthaka ndi pamene wina adzalamulire.
zakukanikani. Perekani kwa ena alamulireeee!
Chatsala kwa inu kumangodya ndalama basi, zotukula masewero zidatha.
Mverani maganizo a ena plz. Tulani pansi udindowo.
nyamilandu has bn there even before I was born, Kodi ufumu wanu udzatha liti, are u The life president of FAM? cannt u see kut u are The failure? bolatu Netball association of Malawi, koma Mmmmmh mwatikola imwe dada nyamilandu, Plz resign.
Kod ufumu wanu ukazatha, Kinnah adzakhala mfulu?
When are you Walter also leaving FAM?? Do you want to do so through a ballot? Nanunso muzisiye zakukanikani, actually you are speaking for FAM when you say Change is good. We surely need change at FAM
Next to go is this FAM Chairman. Perhaps someone more innovative will come up rather than a this lethargic chap.
Nanga inu a Nyamilandu bwanji munakaniza that change at FAM? siizi muti no more CHAN and AFCON? Charity begins at home…..but should not end there. Kusesa m’nyumba sayambira pakhonde bwana Manda, choncho before taking the broom to CAF mudakayamba ku FAM, tele inunso mwalephera ku FAM, patsani ena ayendetse ngalawa….
Nice to have voiced that but dont you know that you Walter Nyamilandu also need to be changed. You have overstayed at FAM and you need to bow down from the seat. Tioneko nzeru zina inu zanu pakutukula football in Malawi zinatha. Kukhala ngati ndi wandale.
GOOD EXAMPLE FOR YOU WALTER NYAMILANDU – ZIMATHA IZI