Email a copy of 'Nyasa BB hold Malawi Carlsberg Cup victory parade: ‘Kuti Nomads ipsye mtima’' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Nyasa BB hold Malawi Carlsberg Cup victory parade: ‘Kuti Nomads ipsye mtima’' to a friend
The Anti-Corruption Bureau (ACB) has changed its plans to jointly charge the three suspects in the Zambia maize import scam,...
musalalate kwambili coz mukudziwa mmene noma imamenyela, to say the trueth, noma inamenya mpila wa bwino kungoti mwayi sunali kumbali yawo,,, sorry for this …………… mabankers nde ifeyo
Mpakana kuti Neba apsye mtima, koma guys neba BP imupeza ndithu makamaka super league ikamuphonyaso !!!!!
Tili mbuyomo mu super league tikukudzulaninso. If you were the best why are you failing to beat teams like us BB? basi kuzolowera kukhalira ana koma ife akulu anzako ukuswedwa
Kkkkkkkk kuti noma iphyse mtima
Stand up for the champion !
Nyerere zili busy ndi SUPER LEAGE osati za anazo lol
Hahahahahaha za ana? kupsa mtima kumeneko! Personally am so glad it ended that way. Mumayankhula kwambiri before the game. Ma player anunso ankadzimva ngati atenga kale Cup game inakali ndiye batali lachita bwino ndithu. Be careful in the league because teams will be coming hard on you….. And mark my words things will not be that easy for you.
Zampira izi kuti neba azipsa mtima kkkkkkkkk!
Super League samadziwika otenga mpaka last minute achimwene, apo biiiiiii mudzakhumudwanso
za akuru akuruzo paja zimakubvutaninsotu kutenga kkkkkkkkkkkkk. chitengere super league sister wnga asanayambe primary school pano ali form 2
League suungaithe nebour