Email a copy of 'Nyasa Bullets supporters dress coaches with suits' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

18 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
Nicho Mlomwe
6 years ago

Mwachita bwino amachititsa mwanyazi pa ground zovala kumangonukha fodya wa mkulu

Eliya
Eliya
6 years ago

ndi ku Malawi kokha kumene izi zimachitika zogulira sokosi ma coach chi ku mangalande mmmmm kulibe kuzambia so mmm sinamvepo kaya mwina ku Joweni ko komaso mmmmm ndakayika

7777999
7777999
6 years ago

Give them good salaries. Period. Nsanje yachaninso.? What is it that is special in other countries that we can not do.? Myopic thinking will take us nowhere. Worshing out poverty is what is not helping Malawi. Let’s think outside the box. Open your brains. Raise money and sponsor Kananji to go for a high level coaching course to enable him qualify to be a full coach osati kumamuyika kumbuyo kwa ena. Empower him for the good things he has done to the team. What is a suit? Azibvala ku church? ?

oMachemba
oMachemba
6 years ago

Kikiki Achina Kananji akuonekabe shapu apa.
Koma ku Malawi kuno ziliko! Mpaka ma coach ndi a mamanger a sports mpaka kukatenga ma suit ku kaunjika? Can’t afford to buy even a descent suit … and they serve professional teams?
Koma abale inu eh?

victor
victor
6 years ago

Good gesture from BB Supporters let those who are talking bad about this good thing Nsanje yakula who told him the Yasini alibe suti kusayamika yanjiru ………………..

ananveruwa akumalowa
ananveruwa akumalowa
6 years ago

7777999 Ndiwe wa nsaje uzafa choncho do you mean that if somebody comes to you with a gift you can say no I have money to buy this one ? ndikufuna uphunzire ichi ineyo ndikunena ine pano ndapasidwa slipas [pata pata] yokuti pa Counter ndi K850 yokha basi komatu ine ndiri ndi kangachepe mthumba mu koma ndalandira ndi ntima wanga onse ndamuthokoza operekayo komaso kuti aziwedi kuti ndalandira ndi mtima onse atangondipatsa ndina vula msapato zanga zodulatu ndikuvala pata pata yo pompo 3 days osaivula kuti ndikamakumana naye azindiona nayo ndipo azinva kukoma, kuti azachitireso ena chimozi mozi ndiye iwe… Read more »

7777999
7777999
6 years ago

Bwana Kangoma ndikanayamika if their take home was increased to K1.5m. I think yogulirana zobvalayi ndi maganizo a chi Malawi. 50 years after independence we think buying a suit for someone is something to write about. Malawi is the only country where football players and coaches are robbed by so called officials.
Malawi is the only country where people worship their poverty. Malawi is the only country where football official’s milk teams .

Kada
Kada
6 years ago
Reply to  7777999

Mwanama amwene,,,, while we acknowlege the challenges malawi football fratenity faces, we cannot downplay the gusture by the supporters. It ndi umunthu ndithu. A sign of love for their team. Great thing bigin with small things like these. Taking responsibility

goodwellbanda
goodwellbanda
6 years ago

Mmmm mpaka ma pant kkkkk

Ngambwe
Ngambwe
6 years ago

Thats why i love this team and its supporters.. ma team enawa anapanga liti zimenezi?? inu a 7777999 muziganiza bwinobwino musanayankhule musamayelekeze m
za ku malawi ndi maiko ena omwe chuma chawo ndichosiyana kwambiri ndi ife. Go maule go!!!!!!!!

mike b
mike b
6 years ago

mwaiwala kuwaguliraso ma panti a red

Read previous post:
Mutharika in game-changing commitment on malaria fight in Malawi

President Peter Mutharika joined world leaders at the Malaria Summit 2018 in London in expressing game-changing commitment to halve malaria within...

Close