Email a copy of 'Nyasa Bullets trim Mzuni to size: Sulom kick-start campaign against albino killings' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

2 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
Major Phaiva Dhandlada
Major Phaiva Dhandlada
7 years ago

ZOONA MAULE TIYENI PAULENDO WOKAMENYA CAF PAJATU TINANENA KUTI ENAWO ANGOTSOGOLA NDI CHIKWAMA KOMA ULENDO SIWAWO.IFE MASUPPORTER MUKUTIMVETSA KUKOMA KIP IT UP BULLETS PLAYERS!!!!!!!!!!!!!!

MAVUZO WA SUPPORTER
MAVUZO WA SUPPORTER
7 years ago

maule woyeeeee,congrats bullets players ngakhale akukumenyetsani mpira wa udzu. Kodi mumamva bwanji mukamawazunza ma players a KEVIN MOYO NDI GULU LANU? CHONDE AP[ATSENI NDALAMA ZAWO MA PLAYERS.PEMPHO LANGA KWA COACH NDAWA CHONDE CHONDE TEAM YOMWE MUNASEWELETSA IJA IPITILIRE MUSAYIWONONGENSO TIMAFUNA MPIRA ADZIPATSILANA FROM THE BACK NDIPO ZONDA KIP IT UP UKALOWA IWE MPIRA BULLETS IMAPATSILANA BWINO KIP IT UP.CHIUKEPO ALI NDIVUTO KWAMBIRI NDI WAKHAZA SAMAPATSILA ANZAKE KAYA AKUCHITA NSANJE NDI SULUMBA KAYA? KOMASO CHIUKEPO UKUKHOMELERA MA PLAYERS ANZAKO IWE.CAPTAIN AZIMENYERA UFULU ANZAKE NOT KUMAPWETEKESA ANZAKE.

Read previous post:
Ministry of trade officials killed in fatal road crash

Three Ministry of Industry and Trade officials have died in a fatal road accident that occurred on Friday 20th May at...

Close