Email a copy of 'Nyasa Bullets win piles pressure on KB: Malawi TNM Super League' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

3 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
waves
waves
7 years ago

aliyese ali pa pressure man even a KB nawonso akupumira mbali. iwe chitemangu ukati kuimenyera ndekuti chani BB iyo sikumenya mpira? sikuwina??

Chitemangu
Chitemangu
7 years ago

Pali ka nkhani aka: Fisi nthawi ina yake ankayitsatira Ng’ombe yamkaka powona chibere kukula chikulendewera amvekere ng’ombeyi igwetsa chiberechi ndiye atola ndikudya. Koma, lo! anawuponda mpaka Ng’ombe inakafika kwawo osagwetsa chibere chija. BB isamale isaganize (living on hope that KB will drop points) forget. BB iphunzire kuwiniratu osadalira wina kuwamenyera.

lloyd chimombo
lloyd chimombo
7 years ago

ali pa pressure ndi a Bb not Kb

Read previous post:
Mhub trains 42 girls in ICT and enterprenuership course

Mhub has facilitated training of 42 girls from peri-urban locations around Lilongwe who have been awarded with certificates after undergoing...

Close