Email a copy of 'Nyasa Times win media awards in Standard Bank Cup' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

9 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
Mpezeni Phiri
Mpezeni Phiri
9 years ago

I wish Patrick Simango, Sam Banda & Deitrich Fredrich were also given these awards. But some sports reporters such as Danger of Matindi FM, Francis Tchavi & Charles Chataza are a shame to the journalism profession. Sports news to them is Big Bullets and amachita kuwonetsera kuti they are Big Bullets supporters.

khasu
9 years ago

Patereki simango usiyire ana pa MBC pano kunenerera mpira.Ntchito ndiyomweyo basi.Mmene unayambira muja.Nthawi ya Bakili.Ino ndi nthawi ya Alomwe tsono. Atumbuka alibe malo pamalawi pano. Patrick kwawo ndiku Tcholo.Amati Thyolo paja.

Madududu
Madududu
9 years ago

Zathu zomwe izi…. Big up guys!

Gona n'kuphe sali patali
Gona n'kuphe sali patali
9 years ago

Big up to all winners but stil work towards professionalism

Gona n'kuphe sali patali
Gona n'kuphe sali patali
9 years ago

Bwana Nyapapi pa anthu omwe mwatchulawo ndivomerezane nanu pa Sam Banda ndi Patrick Simango koma achina Chigwenembe, Dedrich kaya mumatiso Danger aaa ana akuononga utolankhani pa malawi awa phada weniweni amangopanga zomwe anthu wamba akufuna osat kuti utolankhani umafuna chiyani nkona pake anthu ena amaona ngat akukhomereredwa koma ai ndithu utolankhani ndi nzeru

Puludzu
Puludzu
9 years ago

Komatu ma judge amenya pose ina yake awa……. Perpendicular to the ground. Wawa ma jaji wawa!!!

Thom Chiniko
9 years ago

Congrarts guys

Malawian
Malawian
9 years ago

I agree that Patrick Simango is one of the best. His reporting is both entertaining and educative. His commentary in Chichewa is just a marvel to hear! He digs dipper and I like his selection of words and his application to sports. Next time also involve people like Professor Alfred Mtenje (a linguist) to be one of the judges. Otherwise Congratulations to all.

Nyapapi brother
9 years ago

congurats nyasa times for making it but next time ma judge wo muzawauze kuti azimveranso maradio ena kuti azaziwe kuti best sports radio reporter si bango ekha kuli achina chigwenembe, sam banda, dedlich fredlich ndi munthu wamkulu patrick simango.

Read previous post:
FAM, Carlsberg Malawi clash over TNM donation to Flames

Official sponsor of the Flames, Carlsberg Malawi has reportedly blocked one of the leading mobile operators in the country TNM...

Close