Email a copy of 'OG Matches dupes Malawians with ‘Moto kuti buu’ promo, CAMA says ‘serious crime’' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'OG Matches dupes Malawians with ‘Moto kuti buu’ promo, CAMA says ‘serious crime’' to a friend
UK based Malawian singer Hazel Mak is excited to join renowned comic star Anne Kansiime at Grajoh Entertainment, a Ugandan...
1. u r hav destroyed the reputation of yo company. matches anu sitizagulanso
2. matches anu okanikanso kuyaka, u cant compete with Leopard
3 wanya nayo mphwanga mmwenye. ukukhala kuno mwachisomo ukutiberanso? uvutika udziwanso sitikusiya nyani iwe.
Musade mmwenye zangovuta basi.
Multinationals are forced to but prizes even before the competition starts….nde izi zatha bwa
A Hanif Osman u MP Mumafuna uja mumaufunila kuti muzitiber podziwa kuti boma likutetezani.Mwenye ndi Mwenye basi sayenera kuyendetsa dziko ku Africa.Come 2019 more Indians are strategising to stand as MPs.We will discover one day that 75% of our MPs are Indians.
Amwenye akutibera dzuwa likuswa mtengo. Wina ndi uja anaba kumtsekera bank amulola wabwera watsegulanso atibere zenizeni. Ziko wanu, ndalama wathu!
Why are u fighti amwenye when TNM pasavute charges 11.11% but lies in adverts that u pay 10% more.a malawi is this (10/90)100 to me it 11.111111% over a million kwacha that’s alot of money.u request 100 credit they give u 90 and u pay back 100 which is 10 more but u got 90 units miss informing and duping malawians
Amwenye don’t take advantage,zoyambana ife ayi,dziko lathu ndi lamtendere thus y lingolemerabe mboni ndi Peter
taking us for granted .
Amalawi ndife ansanje+nkhanza+kuponderezana tokhatokha. Nkhani imeneyi anakakhala kampani imapangitsa mpikisanowo ndi ya wachlokolo (m’Malawi wachikuda),ooh atamangidwa kalekale and atayalutsidwa. Koma poti ndianzathu achimwenye,aaah muona kutha kwake ngati moto wankhuni zaziwisi. Even MACRA is got powers to bring them to court,why going forward then backwards. Hahahahaha!
Sure
Lilongwe CITY MALL SHOPPINGS competition without closing date just to mislead consumers. Displaying a Nissan Note to cheat customers. Tell us when you are closing.Daylight roberry.CAMA find out