Email a copy of 'Painful defeat but not embarrassment -Wanderers' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Painful defeat but not embarrassment -Wanderers' to a friend
The good mood continues for Malawi champions Big Bullets. They are back as the dominant force in Blantyre against their noisy rivals...
a coach timu yathu imachosatu!ife sitifuna kusewerabwino tikufuna kupambana.mufuna tiyankhule chani?Mukumasewera ngat chikho tatanga kale game ija draw yokha tikadakwanisa mpaka ku luza?kananj tikumvera inayi tikaluzatu ooooowooo!
YES WE ARE THE CHAMPION , ENTER CAF AGAIN ,BB YOU WILL NEVER WALK ALONE, ILIKE BB AND LIVERPOOL .
Ana achepa
akuluakulu amanoma yesesani kodi mukufuna ife masapota tizingolirabe? Tizingoti mpira tasewera bwino koma osawina? Tatopa ndi kutonzedwa.
..ukagwa udzuke zisase pitiliza ulendo…simathelo awa,Nyerere will march on!!
Bullets ikusowa saizi! mulira simunathe .Max Bullets ikakuchinyaninso pakuti Maule ndi Maule sachepa.Watch out!!
No matter what but noma for Life for Future. TNM is for noma
napepe nyerere
De bato isn’t over.let us focus ahead.Noma forever.
Nyelele 4 lyf no matter wat had happened