Email a copy of 'Panga-wielding Bullets fans attack coach Ramadhan' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Panga-wielding Bullets fans attack coach Ramadhan' to a friend
Malawi expects donors to to contribute about K40 billion towards the 2015/2016 financial plan, Finance Minister Goodall Gondwe has aid....
Ndiye a Malawi tizaziwa chani guyz???????????
zakuvuta neba. zako usolva.
koma bullets
abale bb yatani musowa nkhani taonani bvuto la team yanu muiwala kukoza mabvoto ama player anu s/l yasala pangono.chabwino ndichimene cimakhala pachanya,bb its a big team in malawi.
apa nde bullets yafka pa ugalu
This is a ruthless attack on Malawi football! Did they think Ramadan was going to resist if he had been asked to leave his job? These people are damaging the reputation of BB, at least in the eyes of the corporate world and peaceful soccer loving Malawians.
This is a very serious crime. Is the trainer taking the place of Ramadan a CAF licence holder as per CAF requirements?
Ndichifukwa chake timati ma sapota a Bukllets ndi makape, Masavegi, Zigawenga, Ngakhale ma players ena. Tikudziwa sionse koma axchuluka ndi mbuli sadziwa spotsmanship. Akudziwa kuti alephera mpirawu.
UMBULI
A Bullets nziwawa izi mukuwona ngati mungapeze sponsor wa mphanvu?? Time to change now! Or mutamthamangitsa lero coach koma mudziwe kuti ndalama za contract mumpatsa zonse plus chindapusa! Komanso anthu okuthandizan achepa!