Email a copy of 'Parliament approves Kachama as Malawi Police chief' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

67 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
MBWENU
MBWENU
9 years ago

Congratulations a bwana Kachama. Mulungu akuyanganireni. Mwayamba bwino poyamba kumanga anthu a ma bottle store amene akupitiliza mpaka nthawi yochedwa ndi kuimba music yosowesa mtendere anthu. Ma bottle store a kwa Mananse , Nancholi ndi Manytowe. Zikomo bwana. Anthu a madera amenewa apeza mpumulo. Pitilizani kuwamanga. Ndikhulupirira mufikanso pa Kamba pamene pamakhala chisokonezo zedi. Ma galimoto amapangidwa park mu nseu blocking other road users. Ngakhale chigololo amachitira pa nseu pomwepo- chopolama pomugwiritsa mkaziyo tayala ya galimoto. Njansi zeni -zeni. Please stop this madness. Ku Kanjedza pa ma bottle a Chisesele kumakhala disco ndi phokoso 24 hours. Police cars are packed… Read more »

Gundumulani
9 years ago

Congratulation bwana Kachama so you better praise God and we shall pray for you

Wampwesa
Wampwesa
9 years ago

UNIMA inali kale people prefer to send their children abroad or atasankhidwa ku UNIMAyo.

Toy
Toy
9 years ago
Reply to  Wampwesa

Which means Shareworld is total disaster

Proff. Ngangabulawayo
Proff. Ngangabulawayo
9 years ago

Zabwino zonse abwana. Koma musayiwale anyamata anu mbuyomu.

POLICEMAN
POLICEMAN
9 years ago

A Bwana gwilani ntchito momwe mumagwilira muja. Inu musakhale spokesman wa police ngati ena aja.

Masiku
Masiku
9 years ago

Zoona akumudziiii…….Congrats…

Mandolo
Mandolo
9 years ago

Bwana IG, ndinamvera nyumba ya malamulo momwe inakukonderani, ndichifukwa chamakhalidwe abwinno. CONGRATS. mupitirize makhalidwe abwinoo.

Happy Eduardo
Happy Eduardo
9 years ago

Congratulations are in order bwana Kachama. Ine Mphunzitsi wanu wa Research Methodology ku ShareWorld Open University. We will talk on phone.

joe
joe
9 years ago

Zabwino.zonse

MPOTOPHWANYE
MPOTOPHWANYE
9 years ago

IG koma uyu

Read previous post:
Mphwiyo insists Kasambara plotted his shooting: Malawi cashgate

Malawi’s former Ministry of Finance budget director Paul Mphwiyo told the court that that former Justice Minister and Attorney Ralph...

Close