Email a copy of 'Pastor Salanje admits being rude: ‘I don’t need Malawians, they are calling me Satanic’' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

89 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
Mtambo adams
8 years ago

Mr u going no way in RSA,unfortunetely you in the wrong place…procced

Truck
Truck
8 years ago

Salanje akunena zoona a Malawi ife tili ndi nsanje .Sitifuna kuona mzathu akutukuka tidakali ndi maganizo akuti amaene angalemele ndi auje .Pamene Mulungu polenga
aliyense anampatsa mwai wake tifune olo tisafune ngati Mulungu anati udzakhala
chonchi ndiye kuti udzakhala chonchi komanso tidzikhala ndi ambition Mulungunso
amathandiza munthu wodzithandiza yekha.

JJ
JJ
8 years ago

The judgment z around the corner.

Chidongo j
8 years ago

Inu a Salanje mukuonekeratu kuti muli pa mavuto a akulu, chuma muli nacho koma sichinga gule mtendere pongonena kuti simudzabweranso ku Malawi zikusonyeza kusowa mtendere ndi po tchubula za magalimoto zikusonyeza kuti munali ndi mangaw ndi anthu ena ndiye mukufuna muwauze kuti or mudane nane ndapambabe. Akazi anu ndi ana anu akanakhala anzeru bwenzi akuti amuna anga kapena a bambo musatero si bwino. Taonani matama anuwo mwalandira nao nyozo ulemu wonse kuchokeratu ndi anthu amene samakuziwani kuti munapezeka ndi ziwaro za anthu mu fridge akudziwa. Mashoni siyinkhala ndi mpanda wotero ku Joni musatinamize. Ndimmene mwaonera nokha ndemanga za a Malawi… Read more »

titus Scoti
titus Scoti
8 years ago

Za pa dziko nzachabe chabe anatero Mlaliki (Ecclesiastic)

mlomwe2
mlomwe2
8 years ago

CHUMA CHOPEZA UTAKALAMBA CHIMAZUNGUZADI MUTU ETI????????????????????????????

Enock simunthuwamba Makomo

hahahahahaaaa mr Salanje sopano pitanidi ku America ifenso kuno sitikukufunani musazabwelenso,M’busa kunyanyala Nkhosa zomwe mbuye wake wamupasa kuti azisamale zoona???

chechipapwiche
chechipapwiche
8 years ago

Signs of the times.

nankhoma
nankhoma
8 years ago

zaziii!! osawathandiza abale anu ku Ntcheu ku Chinkhwamba akuchita kusowa nyumba aja bwanji? which god z this??

alick fwaya nkhatabay boy

Pastor of sineers salanje

Read previous post:
World Bank denies dictating Malawi on financial matters

The World Bank office in Malawi has rejected accusations by some Civil Society Organisation (CSOs) that the institution was dictating...

Close