Email a copy of 'Police arrest 23 people over FISP, Admarc maize' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Police arrest 23 people over FISP, Admarc maize' to a friend
State President Professor Arthur Peter Mutharika on Saturday attended the national prayers which he had personally called so as to...
Akapezeka Amangidwe Basi Ndipo Apatsidwe Chilango Chokhwima.Komanso Ndizomvetsa Chisoni Ndizamanyazi Kuti Akumayambitsa Katangale Ndianthu Amaundindo awo. iiiii!!! Koma Nane, Kaya Ndaganiza Bwanji Kaya, Shaa!!! Basi, Zagwa Zatha.
Mmudzi wa nguluwe T/A Bvumbwe mpaka pano anthu sanalandilebe fertilizer,chonde tithandizeni kufufuza.
Ndithokoze apoliice tayesesani,chifukwa zimenezi zikupweteka amphawi
Ndie maboma omwe akhudzidwa kwambiri ndi kwawo kwa Bwana Muthalika ena akuti kumenekunso ndie kwawo kwa kuba ndi katangale .
Komano ndizonvetsa chisoni kuti mukuwachititsa manyazi bwana Muthalika.
THE CORRUPT AND STEALING PRACTICES WILL NOT CHANGE ASL LONG AS LEADERS ALSO DO SAME.
Malawi is still poor shamed country