Email a copy of 'Police arrest Lilongwe head teacher for embezzling MSCE exams fees' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

4 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
Sim Doxsy
Sim Doxsy
6 years ago

Zonvesa chisoni kuwatero ana. Ndye akufuna ana atani amene nthawi imeneyi please a maneb chitanipo kanthu mwa changu

Siyani
Siyani
6 years ago

A phunzitsi amenewo. Sanadziwe kuti akhoza kumanga. Mwina anangidzimwera mowa ameneyo. Koma ndalama take ndiyochepa kwambiri angapange NATO chiyani imeneyi. Be rensiposible, sir. Mwawona mukalo Nazi Ku ndende za zii. Komanso wawononga tsogolo la ana.
Makolo awo amaganiza kuti athana nayo budget ya fizi, iye kuwabwenzela mumbuyo.

san
san
6 years ago

Kuzunza ana uku,kuvutika kuwerenga, kupereka fees wina kungowadyera. Chilango choyenera ndiye kumulamulo kuti atenge responsibility ya ana 19 wo powalipilira tuition,transport,lunch ndi examination fees mpaka adzalembe next exam. Mfiti ya munthu! kuzolowera nyau basi,usandilankhulitse pambali mwana wa Chimbano chidzukulu cha Kangw’ingwi.

siphelele mthembu
6 years ago

ochewa

Read previous post:
Gym equip up for grabs in Standard Bank ‘Be More’ race

As countdown to Standard Bank “Be More" Lilongwe race scheduled for July 30, 2017 continues, Standard Bank has dared prospective...

Close