Email a copy of 'Police chief to form commission of inquiry over Buleya Lule murder' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

12 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
Innoxy
Innoxy
4 years ago

I’ve got some proof that politicians in malawi are above the law.That’s why we are experiencing these nonsense.Malamulo a dziko la malawi amagwira ntchito pa anthu osauka awamba but remember that there’s almighty god who owns anything including nkhalamba yotchedwa MUTHARIKAyi.

Innoxy
Innoxy
4 years ago

Commission of inquiry would only dash in if there was no clear evidence of those police killers.You know who killed that man and yet malawians should expect nonsense from that commission of inquiry???. Who do you think you are and why there is injustice and lawlessness in this country or how do you regard fellow malawians??.Note that there’s almighty god who has promised to deal with such kind of people and the day is coming and whatever you enjoy at this time is infinite.You will rot in hell together with those politicians.Killing your fellow malawian just because of money?, where… Read more »

PHANANA
PHANANA
4 years ago

INQUIRY FOR WHAT STUPID ZINTHU ZOWONEKERATUZO

mada k
4 years ago

yachaninso abale!!!! anali pa duty ndi ndani si basi nkhani yatha? mpaka commission of enquiry? or mwana waku primary nkhani iyi ingamutengere 1 day to finalise? mxwiiiiiiiiii

mtete
mtete
4 years ago

A Commission of Enquiry instituted by police to investigate death in police custody of any citizen does not inspire confidence at all. The issue is made worse when the person at the top is implicated in wrongdoings such as Chasowa murder.

Bito
Bito
4 years ago

Useless and stop the nosense. Commission of inquiry for what? This country is fast becoming a lawless state because of these bastards.

ananveruwa aku veterinary ukoo nsewu wa midima
ananveruwa aku veterinary ukoo nsewu wa midima
4 years ago

Miyoyo yathu ifeyo siya DPP kaya MCP, UTM, PP, UDF. ayi sopano mwanva komaso inuyo apolisi muziziwa kuti ifeyo as Malawians sikuti timakuopani ndisaikemoso malawians no ineyo pandekha sindimakuopani antaa olo pang’ono koma timayenera kukupasani ulemuwanu pantchito yanu ndinu ofunikira kwa ifeyo komaso ifeyo ndiofunikira kwa inuyo chinaso ziwanikuti lero ndine civilian mawa ndizakhala wapolisiso bwino bwino kapena wa Army inuyo mutachotsedwa do you mean that ndizakuzunzeni chifukwa ndalamulidwa ndi andale to do so? never muziima pa chilungamo A Rodney Josey, ndipo mumudziwe Yesu pamozi ndi ophunzira ake onse 12 muziima pa chirungamo osamapembeza milungu yakufa mwanva timakulipirani ndife osati… Read more »

ananveruwa aku veterinary ukoo nsewu wa midima
ananveruwa aku veterinary ukoo nsewu wa midima
4 years ago

Akulu comishoni of inkwayale yachani kodi munayambira muja pali chanzeru chomwe timaonapoi? aphwanga apolisi muziziwa kuti moyo wamunthu sioseweretsa mwanva Mulungu sichitsiru popanga moyo mwanva kunalitu anzanu Achimbayo, Achigawa , Aziniso ndiena ambiri Kamuzu alikuti zachiziwikire kuti munamupha Buleya Lule njauju chatsowa koma Mulungu alindimaso ndipo saodzera komaso tsikulina kunoko kuno Ku Mlawi kudzachitika chipolowe choti Apolisi nonse simudzakhulupirira inu pheeeee zimandiwawatu

Njolo mpilu
Njolo mpilu
4 years ago

So ija anapanga pitala ija yatha bwanji inquory komishon.
anthu mwabaizika. Stop fooling us and looting. Mubise ndalama mmatumba a ma komishion
Mxiii.
Vimitu etu

Tchana
Tchana
4 years ago

Ma dpp diehards…..dikiran pa 21may .dpp u have failed

Read previous post:
EU observers call for transparency in Malawi elections: ‘Rigging claims mere politicking’

The European Union election monitoring team officials have ruled out rigging in the May 21  tripartite polls, but  called for...

Close