Email a copy of 'Police extract Msungama's mobile phone data: ‘Malawi WhatsApp coup plot’' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Police extract Msungama's mobile phone data: ‘Malawi WhatsApp coup plot’' to a friend
President Aurther Peter Mutharika on Tuesday conferred honour of Senior Counsel (SC) to 10 seasoned legal practitioners among them, Justice and...
Apolice inu mumfunse mukhito amatero pofuna kusangalasa mbwiyake koma atasiya ufa mbwiyakeyo anaona zotani? be careful!!!
Koma m’malawi sadzathekanso ayi, kupusa kuchita kuposa tudzi? Bolanso tudzi limanunkhako anthu mkutseka mphuno. Ofunika kuthamangako mwina mkuchenjelako abale.
Koma ABALOTELI mwanyanya. Mpaka pamenepa? Pafunika kuwapanga hirer ajawo adzakuwumbeni ndi Mitu yanu yonga ZIBOLI. Za Ufiti basi.
Koma tikanathamangako pang’ono nanga chokharila mdziko lopanda chakudya nsi chani mwina tikanachenjelako, zilizonse kumangoti yes bwana jesus its now the time to come coz tikuwonjeza kwambiri its worse than ever.
Anthu otsutsanu nde mukuonjeza kwambiri.ngati ndinkhani yotukula dziko bwanji kungonena nzeru zanu kwa amalawi and working together with the rulling government to develop malawi. You just wasting your time ndimapulani ongofuna kuphetsa anthu osauka coz the end results a mapulani anuwo ndi nkhondo.anthu sanakusankheni with a reason behind so give chance to the DPP .please please musatiphetse!!
the information deleted can easily be traced if really someone wants it, nothing has been done here with the advanced technology!!!!!
Is it right for the policemen to snatch my phone and read my privacy? This is happening mostly at Kanengo.Where to they get these rights?
koma anthu inu….
dont dare doing things or starting things u wont manage to end it….because what u are doing will lead to something that will not be good. Damn Malawian politicians dont u have well planned strategies for your psrties for 2019?…apart from planning to pull somebody down? sit down and get back to your senses, think about your relatives, friends and families when cold war starts…because what you are doing can 100 percent lead to that.
ask rwanda…u selfish vagabonds
If left alone, the Malawi Police has no capacity to convict the accused. They are just wasting their time. How will they prove to the courts that the data they have collected was indeed from the said phone, beyond reasonable doubt? Besides, if someone refers to the Egyptian incident, no one overthrew Mubarak, but all disgruntled Egyptians through demonstrations, which is also a constitutional right in Malawi coming as a right of association.
Vuto ku Malawi dyera inu achipani kuyikira kumbuyo zoipa. Dzana anali Peter ndipo mudatukwana police. Mawa mukakhalanso inu muzatinji?