Email a copy of 'Police quiz Lutepo’s wife: Kasambara, Manondo now face K785m cashgate charges' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Police quiz Lutepo’s wife: Kasambara, Manondo now face K785m cashgate charges' to a friend
Malawi First Lady Gertrude Mutharika has been invited to be a Guest Speaker and panelist during the Women's Entrepreneurship Day...
I want to c these guys locked up and shame on Kasambala and Manondo they wives ll be enjoying with there boy frnds
Amalawi tiyeni tisiye nkhaniyi. Chomwe ndikuwona apa ndikusangalatsa azungu. Pano dzikoli tikuyendesa tokha ndi misonkho yathu, bwanji tipange maintain zero dfct. Koma boma liyike controlling measures. Azunguwa atizolowera. Ma victim wa akawina boma lidzawononga zambiri kuwapepesa.
Ndatopa ndi nkhaniyi ndikufuna ndisiye kuitsata. Jail these guyz then muone umo malawi asinthilenge.
Kasambala winning
SORRY NDIKULEPHERA KUNENA ZA IZI SHAME !!!!!!!!.
All involved in the cashgate scandal should be arrested and their ill gotten properties be confiscated.The bank managers should also be taken to task without questioning such collosal sum of money entering into these thieves accounts.Why do we Malawians worship thieves?They should never see sunlight in their lifetime.Lock them up and throw away the keys in shire river.
Masalamusi awu Munthu, why involve your family in this Manyi ??? I wonder
Na apa RK walowa kale ku prison…kkkkk…when you come out mkazi wako ali ndi baby wa 10 years old.
Mwatizolowera Mwamva!!!
kodi ma banki manejala amapereka vindalamavo muwatani? nili udabwatu ine zedi. nimasuleni.
ndine wakumudzi ndiye sinzitsata kwenkweni za m’ma bankizi koma nimanguyesa kuti vindalama votapa vikachuluka, obwana obankiwo omayenela kudabwapo kanthu nkuletsa kutapako nkunena kuti vachuluka vima wanisauandevi tikumangani pompano