Email a copy of 'Police raids lead to arrest of 6 'vicious' gang members in Lilongwe' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Police raids lead to arrest of 6 'vicious' gang members in Lilongwe' to a friend
At least 42 people have been arrested for allegedly being involved in looting shops at the gutted Mzimba Market which...
Apandidwe amenewo
Anyetseni amenewo akuwona ngati kuno ku Nigeria koti angayambitse Boko Harram.
Atumbuka samakhala wonyasa nkhope ndi gule amaneyo
Mapaziwo ndi gule wamkulu wopita kusukulu samakula choncho zilombo zimenezo kapena mizimu
mwadyapo
Koma mtundu wa chitumbuka palibe pa list. Tiyeni tiwayamikire anzathu. Anzathu anapita ku sukulu.
enanu mukuti ndi a MCP amenewa chifukwa choti ali pa Central kumeneku ndiko kulakwitsa kwambiri inu simukudziwa kuti mbava zochuluka ndi za DPP motsogozedwa ndi pitala? mwana amaona zomwe kholo likuchita.
pa anthu 6 palibepo wapolisi ndiye sizinayende bwino. dont be cheated momwe tikunena panomu, amenewo atuluka kale asatinamizepo apolisi apa. akaba amakawapatse iwo omwe. check in their houses they have very expensive things
Achipi, kuchoka kumudzi kuno kani mumathamangira zimenez ? pepan kwambiri, znali zakanthawi kochepa
That is the way to go if you want to win the war against crime. Be conducting raids when least expected. raid markets, bars, taverns etc. Criminals are all over.