Email a copy of 'PP don’t be ‘crying babies’ – Lucius Banda' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

97 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
lucius kholomana muguliwa
lucius kholomana muguliwa
9 years ago

Lucius wayambapo waiwala zake zija

Imraan Sadick عمران صادق

Crying babes ha ha ha ha ha ha ha ha ha!
Pepani a PP ife sitikuthandizani kulilako za Cashgate sitimadya nawo kkkkkkkkkkkkk

Makwinja
Makwinja
9 years ago

Wise saying lucious. They are really crying babes

Revelation kamanga
9 years ago

Just comfort them and it was not they time!

nkhakamila
nkhakamila
9 years ago

vuto ndi loti a malawi timayankhula za mavuto a anthu tikakhala kuti sitili pa mpando.Banda is right.zimakhala zondiwawa ndikamakumbukira mmene ndalama za cashgate mmene zimamwazilidwa.who cared by then ndi cash gate yanuyo kuti anthu akuvutika.muzipatala munalibe ndalama.motchale yeni-yeniyi mitembo ya anthu kumawola chifukwa choti compressor yapsya.a malawi tisakhale a mzeru lero.zinthu mziko muno zinayipa kale.Bravo to you Lucius for ur comment.thats maturity in politics.ngati kuli kudyerera bwana pangani choncho ndi nthawi yanu.enawa anadyerera kale za cashgate mu nthawi yawonso and tonse timawona.ena anachita mpaka kuzipha chifukwa cha mkwiyo poziwa kuti zawo zawadera cashgate yatha after kuluza. lucius woyeeee….thats southern behavior.anthu… Read more »

Chris Namilaza
9 years ago

Izi ndi zimene amafuna a Mbendera monga momwe ananenera a Mbendera ku Tally Centre.

Ndigida
Ndigida
9 years ago

Wise ones will take the advise from Lucius Banda but fools will ignore it.

public taker
9 years ago

Kodi certificate yabodza imene udalinayo ija, kugwilitsabe ntchito? By the way, who is L, Banda? Is he a politician, musician, or garden boy? Lusiyasi, is nothing @ all. In short, pankongo pamako wanva!!!!

Vekere wavekere
9 years ago
Reply to  public taker

Iwenso public taker tinene kut sumamudziwa,Lucius?Nawenso nzeru nzoperewera ndi2

Aceton
Aceton
9 years ago

Owerenga khala maso.Kodi mabvutowo ali ku Malawi kokhako?

unedyo
unedyo
9 years ago

kodi form 4 unakhonza tsopano???????

Read previous post:
Edingeni secondary school gets 85 desks: Inkosi M’belwa hails Airtel Malawi

The romance between Airtel Malawi and the country’s education sector is getting sweeter, better and bigger. On Wednesday, Airtel took the romance...

Close