Email a copy of 'Prison boss reveals why he shot dead his son: On bail' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Prison boss reveals why he shot dead his son: On bail' to a friend
Malawi government has been asked to press for compensation from the South African government for its citizens who are victims...
why? now mr chisi you have been a role mordel 4yrs
Mr chisi siolakwa ayi,baibulo limanena kuti mwana osamvera makolo afe ndithu .
From the look of things, the two sons deserved the punishment. Why? How can a 29 year old resign from work and opt to stay with his father? This clearly explains that the father was so loving to accept this idit to come back home. . My advice to the courts and those doing investigations. Find out from direct relatives on how these two bustards used to behave, Extend to neighbours and their closest friends.
Mdala yu analakwa pa lupha ndi mfuti koma mukadakhala enanu mukadalolera kuluza moyo wanu after spending your money on the two stupid sons.
Mwana Osamvera Kholo Afe Ndithu
ana mwaonjeza masiku ano, mwana osamvera makolo ake mphoto yake ndi imfa basi, koma mr chisi mulape pansi pa mtima wanu, zinangochitika koma sizinayenera kukhala choncho
Zoona zake ndizakuti mdalayu anangonana ndi mwana wakeyu ndiye anyamatawa zimawasowetsa tendele chifukwa amkafuna kuthana ndimdalawaoyu
Oooo!zamasiku ano izi.
Anawo analakwitsa inde koma mpakana kupha?Ayi ndithu Yehova atithandize.
Walhai, a Mjomba Chizi anaonjesa! Ngakale Baibuli olo Curuan imakana simenezi. Imeneyi si Jihad!
Ephesians 6 : 1 Children Obey Ur Parents In The Lord For This Is Right. Mr Chisi And The Daughter Has The Truth Of The Matter.