Email a copy of 'Prophet Mbewe ‘prophesy’ Vice President convoy accident' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

36 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
winston msowoya
winston msowoya
7 years ago

F0r God’s sake,these people are not Prophets, they are thieves and lions in sheeps’ skins.If this guy was a Prophet,how could he fail to foretell the predicament that awaiting the VP? In Malawi whom should we trust? The President himself is a thief,his Ministers are thieves and the MPs are a bunch of idiots.OH! LORD,DELIVER US FROM THESE SATANS!!!!!

Lemekeza
7 years ago

Baba Chilima musatekeseke ndi anenere onyenga ngati Mbeweyu, Akapanda kunama adya chani pa town. Kunamako ndipo podyera pake.

Whatnext?
7 years ago

So how will one pray for a country which he/she doesn’t know? Praying in vacuum? Isaiah, Jeremiah, Samuel etc, the bible prophets we know never beat about the bush when revealing a prophecy to people. I am baffled why today’s prophets are so afraid to tell us specifics of their so called prophecies. Are they even not sure of their own prophecies? Are they afraid of being found out?

Who we be
Who we be
7 years ago

MA pali Mauritius Mali Mauritania etc. Prophecy iyi is targetted at our own innocent VP. Zazii basi.

Betland
Betland
7 years ago

Mukati simuna ntchule zina inu muli dziko lanji? Ndipo chakupasani inu chimdi ndichanu kuti maganizo anu asanduke ulosi powuza dziko. Inu tazingowabela anthu amulungu koma zenje lanu lili pamovuto ndipo sinu neneri. Palibe neneri yemwe analosela kubadwa kwanu. Uthenga oti inu mwabadwa aunabwera ndi gogo wina zina lake Sanudi kukawawuza Malo anu kumusa kwa msewa. Chonde chesani.

Betland
Betland
7 years ago

Kod ngati inu muli neneli ndi buku lanji likamba zakubwera kwanu! Ndipo ndichizindikilo chanji chomwe mulinacho? Poti nanga ndibuku lanji mwaza nalo lokamba za inu kuti ndi neneli Oh Mbewe upezeni mtima Buku loyera mumapezeka pa Mateyo 24:4 pepani simuzaziwa za mawa. Ndipo inu Mumwalira or patalike bwanji ndipo mukaweluzidwa pomulosela nzanu zonyasa. Kodi ndinu opambana kuposa Angelo? Mafupa anu 360 pomwe Ngelo sawelengeka. Nundi kapolo wa Mulungu Allah dekhani ndipo zinena zowopa mulengi Allah

Betland
Betland
7 years ago

Ndichifukwa chani simalota zoti baja lawujeni lizasangalala polibe yemwe amaziwa za mawa ndimulungu Allah ekha. Mateyo 24:4 onyenga awa ife timufunila zabwino vp. Ndipo atetezedwa.

Raw Stuffer
Raw Stuffer
7 years ago

Kodi za mkazi uja anapasidwa mimba ndi mneneri David Mbewe zili pati?????

kanga ndiwamba
kanga ndiwamba
7 years ago

bwanji osalosa za bvula mkumangolosa zabofza .kodi anamuuza kuti nfi Mbusa ndani

nyapapi
7 years ago

Mudziona simunati

Read previous post:
Signs of times in Malawi: The ball is in Mutharika and DPP court, now or never

The million-dollar question is whether or not Malawians will ever have a bright future-a future where parents are able to...

Close