Email a copy of 'Radio Maria needs K70 million to extend its transmission in Malawi' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Radio Maria needs K70 million to extend its transmission in Malawi' to a friend
Surely any person going to work outside their country is an expatriate? But no, the word exclusively applies to white...
If all the three Million Catholics were to contribute Mk 1,000.00 each this project would not be a problem at all; ngakhale Mk 500, ndi ndalama zambiri to put up this project and sustain the running of the radio for quite a reasonable time. We do allot of contributions in our Parishes, this could be done!
Kindly consider Muloza-Limbuli in Mulanje
Tisonkha za mpingo wathu izi.
Zimenezo ndiye zofunikazo radioyi ifalikire ponseponse .May God bless u Fr Joseph Kim Amen.
Zabwino zonse , Fr Kimu you make me proud and i really admire your hard working spirit. Please never be discouraged in all that you are doing for the Church and the country. May the Good Lord, the Almighty bless you abundantly.
Makamaka muganizire ku Chizumulu ndi Likoma Islands. Ndi kumene kungatalikirane ndi ma transmiterwo. Feasibility study please!!!!
Komaso Kwathu Kuno Kwa Khongoni
The story of Radio Maria is such a beautiful story. It is the flagship radio in terms of religious radios in Malawi (not just Catholic radios)……. all because of the hard work of Dr Kimu and his team. BUT, do we need 4 catholic radio stations in Malawi (in Mangochi, Lilongwe, Mzuzu and Karonga)? Do we call that a United Catholic Church? We read that in RSA, the Catholic Church which has over 50 dioceses has only 1 radio station – what’s wrong with us? If it is a question of languages, I am sure Radio Maria can accommodate all… Read more »
Pitilizani ntchito yabwino yoweta nkhosa za Ambuye ndipo Ambuye Yesu yemweyo azikudalitsani. Ma ulaliki ndi maphunzitso anu amatitsitsimutsa. Timakunyadilani koma chonde kunonso ku Mchinji mutiganizire chifuwa timamvera wailesiyi movutikira kwambiri. Mulungu apitize kukudalitsani ndipo mupitilize kutipemphelera zikomo.
Ngati n’kotheka muganizirekonso kuno ku kasungu pa boma. wailesiyi simveka bwino.chonde bwerani mudzafufuze.