Email a copy of 'Rangers end BB’s unbeaten run: Malawi TNM Super League' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Rangers end BB’s unbeaten run: Malawi TNM Super League' to a friend
Nation Publications Limited (NPL) on Saturday organised a Mother’s Day Fun Run in Mchinji where they partnered with several organisations...
wether u like or not league ndiya BB FC
Ife a noma, kukoma kunabwelela ife, team yathu imawina munthawi zofunikila zokhazokha….ndichifukwa chake sitinasankhe unbeaten record, mmalo mwake tinasankha finals…NOOOOOONA WOEEEEEE
woyeeeee!
Tsopano iwe botokhoswe, ukut sutsata mpira wapa malawi? Nanga pa nyasa time-pa ukufunako chan? Ndikudabwa pot apa sindinaonepo ‘update’ ya laliga, bundez liga, italia sere A, khaleso english premier. Next time before u talk, you wil make sure that your tongue is well connected to your brain!. I know kut ndiwe wa bullets yogonja, koma Mbambadi theradi ndakwiya nawe kwabasi, unakakhala nane pafupi ndikanangokunyonga basi kut ndikuiwale.
Anyamatawa sing’ombetu iyayi. Musamaname kuti timu mumaikonda musakuithandiza. Mene mwachulukila muja mutapeleka aliyenso k100 ndiye kuti its over k150 mita. Ikhoza kuwathandiza. Inu koma mumamgowabela masaveji! Tchupiti aziluza kumene wamva Rahim
BB mumanyada lindani madzi apite ndipo muziti tadala.
Pepa Burets zimacitika, B4WD taisie ikusesa tima CUP t0seee, reagueee, wat F0R,,,, 0v0teredwa wamkaka iwe tuuuuuu, zak0 iz0 uis0va,,,, kkkkkkkkkkkkkkkkkkkk,
Botomani is describing those who follow TNM as umphawi??? Shame on you bro because kwanu nkwanu. We all follow other teams. Some of us live in Europe but still follow our local football because thats our local flavour. Si umphawi mkulu koma patriotism. Thats why if you go to England you find that teams in championship, league 1,2, conference they all have supporters because those are thier local teams.
Iwe wanoma usayankhulitse wamva???
Bola ukudziwanso kuti iwe si saizi mu ligi. Remember u can only be relegated after kulephera mu lig not cups.
In addition, muluza ndalama zingat mutalephera kutenga ligiyi chifukwa ma fixture onse nchimodzimodzi???
U r specialists in failure nde kuwina game imodzi ife ndi kuluza mu cup ndi mu lig mutisokose??? Mxiee! Jala pa mulomo neba.
Masanje ampira pa Malawi. People still follow this substandard football league, umphawi ….chani ?
mwanya!!!!!!!!!! mwanyanya kuyelekedwa. fulish . unbeaten run? now ur on beaten run.