Email a copy of 'Ras Chikomeni declares he'd be a better president than what Malawi has now' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Ras Chikomeni declares he'd be a better president than what Malawi has now' to a friend
Opposition legislators are pushing for a report in parliament which details corruption at Electricity Suuply Corporation of Malawi ( Escom,)...
Kikikikikiki! Upulezidenti si ntchito yophweka. Sinkhani yachamba ayi. Zambiri zikufunika zikhalepo. Mavoti adzawapeza kwa anzinzake a weed! kikikikiki!
no facts at all legalization ya chamba basi mpaka kufuna kukhala nayo president just to legalize it? What next after legalizing chamabacho rasta?
kkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkk aMalawi tiyese kukhala ndi presedent wa chi raster chamba chidzakhel mbweeeeee aliyense kumangopenga mmene akufunira bassiiii
Ndi mmene alili akulu awa kumamutchalenga Peter muthalika, ndiye kuti utsogoleli pa malawi siuli bwino
INDEPENDENCE CAME TOO EARLY
WE SHOULD HAVE WAITED !! LOOK OUR FRIENDS IN SA — THEY HAVE BENEFITED ALOT FROM MZUNGU — THAT’S WHY WE ARE FLOCKING TO SOUTH AFRICA LIKE NOBODY’S BUSINESS —
bola wachanyu zikamavuta tizaziwa kuti tinapanga great mistake,
bola wachambayu
Zachariah basi!
Let us suport him
Wanyamula running mate wake manja
Kkkkkkkkk wanyamula running mate wake manja