Email a copy of 'Rev. Chimwemwe Mhango shakes Livingstonia Synod, CCAP pastors and followers defect in Karonga' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

26 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
Chibwana J.
Chibwana J.
7 years ago

Who is Chimwemwe Mhango to shake the Synod. If 2 pastors rebel against the Synod basi Synod ingagweee? He shud go back on to his drawing board yaaa!!! plant your own Church umawona a Synod amakuyankha mbwerera zako umabwebwetazo? You shud be ashamed of yourself. Time will come when you will pay for your deeds, believe it if you know law.

kambito
kambito
7 years ago

Some people who are against Rev. Chimwemwe Mhango will still write bad about him. Kuonetselatu kuti sizamulungu.. Munthu at no time o ever heard him kunyoza Livistonia Synod but thanking them kuti ndimakolo ake, anamthandiza.. Za Mpingo Wa Kanengo tose tikudziwa kuti akupempherabe momwemo chifukwa a khristu akuti adamanga okha pamene synod ikuti amamanga pasi pa synod yi..thus why inapita Ku court. Ena akuti they will chose to use force, why people of God? Ndiposo ndi kuopseza chabe kutengela kuti ochuluka ndi ati. Let’s just leave this God’s hand kuti ndizochokela kwa iye let it be, chifukwa ndi maso athupi… Read more »

Gilbert
Gilbert
7 years ago

whether in CCAP or Redeemed, you just an organisation branch and not a church. it God to come in flesh, suffered and shed His blood on the cross to buy His church Acts 20:28. His church is to be known upon His name Acts 4:12. Just think with with me “Redeemed” means to buy back. we see this first in old testament when the Israelites were made free from Egyptian bondage, which was foreshadowing the demption Christ has made to all nation and you think its a name for a church. there is only one church Christ died for Matt… Read more »

Cathbert
Cathbert
7 years ago

wakumanya vyose ni Yesu

Mwakafyali
Mwakafyali
7 years ago

Iwe umalemba article nzeru ulibe kuonetseratu kuti akupatsani sikono mutsamwatu ndi bodza. Paja amalolera kuyitana atolankhani nkuwauza zoti alembe just to advertise his church. Ali pa chi jobs nkulu uyu. Akatopa anena.

Kajililwe.
Kajililwe.
7 years ago

A Livingstonia Synod natu mwamuweta kokwanila munthu uyu ka muthamangitseni mu building yanu. Mungomusekelera adzichita phada munyumba yanu yaku Kanengo? Munthuyutu amadzitama kuti iye ndi celeb ati amadziwana ndi onse a judicial, eeeeee!!!!!!!

Henry Phiri
Henry Phiri
7 years ago

Chimwemwe Mhango yavuta ndi ndalama akuti adzikwerela ndege kupita ku States. Ine ndi mboni ndinali momwemu munthu uyu amatinamiza kuti ayi dikilani tikukambilana ndi a kulu akulu ku Synod. What next ayi akuchita register dzina lina la church, ayi akusintha uniform ndinawona kuti munthu uyu mwano wokana transfer anali ndi chilinga ndipo amafunu agwirits ife ntchito. This is not surprising Chimwemwe Mhango nthawi yina ndi ma frastrations ake anayambanso ka Church kake ku Mzuzu kadakanika pano wati akatole mpingo womangamanga wa Kanengo. Ambuye mukantheni M’busa wonyenga uyu.

Kajiso Disi
Kajiso Disi
7 years ago

Linda Khonje nawe bwanji sukumuthandiza nzeru uyu crook wakoyu? Ndani muma saloon atsikana samudziwa Chimwemwe Mhango azimai? Pompano umva timakuwona ngati wanzeru mai koma nawe dyera landalama lakuvuta. Mai opusa usadzati ine sindinakuchanjeze.

Mgemezulu
Mgemezulu
7 years ago

This so called man of God Chimwemwe Mhango is too crooked. He is money hungry. Ask him as to why he is still housing his church in the building belonging to Livingstonia Synod? Changing the name of the Church, changing uniforms in the building which is not his. If he is man enough let him leave the Livingstonia building and stand alone. Its where he will test if all those in the building belong to him. He hates people who are trying to put sense in him to leave the building. All this is because the Supreme Court of Appeal… Read more »

Mswazi
Mswazi
7 years ago

Ndalama ndiyo yasuzga apa.

Read previous post:
Mutharika wants Chaponda back as leader of House: DPP Divided

President Peter Mutharika wants the embattled Minister of Agriculture, Irrigation and Water Development, George Chaponda to be reinstated as Leader...

Close