Email a copy of 'Robbers attack Muluzi residence, two watchmen arrested ' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Robbers attack Muluzi residence, two watchmen arrested ' to a friend
Ireland President Michael Higgins said he has seen for himself the “warmth” of Malawians with the good reception he received...
The Police are missing it all. Main master minders of Crime in Malawi are PMS guards . There is Phiri who is still on Police pay role yetbhe is on the run bussy with robbery activities. PMF guys are hungry for money and would do anything to conive with thieves. look st the Mzuzu bank robbery, a Pmf guy drove all the way from BT to facilitate crime I. Mzuzu. pa C company ib LL ndiye alipo ambiri and amadya limodzi ndi ma bwana awo.
nonse amene mykupanga macoment aoa ndinu zisilu mukuchigwira nyanga poti chili kwa nzanu amphawi wankhaza inu kagwereni uko..
Adzidziwa Mwina Amangomva
Apapa nde zili bwino….mwandibanda onyata inu. Nkadakudziwani nkadakupatsani ndalama, mwabayo yachepa
Mwayamba bwino. Odi ndikupatseni list: watsala KALIATI,CHAPONDA,NANKHUMWA,DAUSI,MPINGANJIRA komanso omwe amalankhula mopusa a mphawi tikamalira. Mukadayamba kale kubera mbavazi mukadalemera mwachangamuka mochedwa mmataya nthawi kubvutitsa Amphawi anzanu.PITALA musam’bere kaye akhale Nyambalo yomaliza. Askumangeni simunabe mwakatenga zanu.kungoti simunamuuze kuti mutenga pa tsiku lakuti lakuti.
Ndangothokoza kuti anangoba namusiyira moyo Atupeleyo, that is being professional…..imagine if they had killed him…….what would become of the UDF, the Alomwe and the Achawaz…..the Achawaz would be thinking that Atupele was invited into government so that he can forever be silenced and Mangochi-Sharialand siyinakayimva. Munakunthana nokhanokha!
Mukawabereso plz mundigaileko
YAAAA Kuba koma kumeneku next state house katengeni ndalama zanu zimene nkhalambayi ndi mkulu waka adaba
chitsiru ngati tate wake akanachipha kutengekatengeta ngati maliro anjoka nkutaya.
YAAAA Kuba koma kumeneku next state house katengeni ndalama zanu zimene nkhalambayi ndi mkulu waka adaba