Email a copy of 'Sex slavery: Malawi police rescue girls in Ndirande' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

54 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
Bashir omar wa bullets
Bashir omar wa bullets
9 years ago

Palibe chimene mwapindulapo coz ikalawa mchere basi simafuna kusia ataaa

wadala
wadala
9 years ago

Iwotchedwe asante sana yo. Women in forefront? Zoopsya kwabasi bwanji osatenga ana obereka nokha koma aanzanu?

2mbwe
9 years ago

Not on,it is sad to hear such stories from town where most inahbitants are at least civilised and are able to analyse issues soberly.This entales that this maipractice is rampart in outskirts so the government has to do something to curb the situation.many young girls are victimised in villages but they don’t reveal to relevant staff because of cultural and religious beliefs,please our dear govt,come to our rescue,deploy strategies to even manhandle those who perpetuate this.

omar khaliffa
omar khaliffa
9 years ago

Ku Mangochi nako

mwanawamkulu
mwanawamkulu
9 years ago

Koma tinali bho tianati! Makamaka kakang’onoko! Eee kanali sharp!

mayamiko matapa
9 years ago

Zopusa osatenga azichemwaliakobwanji?

Favour
Favour
9 years ago

Koma uhulewu ndiye wafika pena pake.kwathu kuno ndiye zosanena.Ana a zaka 12,13 ali mbwembwe mu ma bottlestore.Akuti azibambo amalipira K300.00 kuti agone nawo ,just imagine.Apolice ayesayesa kuwagwira koma alephera.Zoopsa kwambiri.

cynk
cynk
9 years ago

ubale ako ana azikwatidwa osati ana akumudzi azikupangira ndalama, mwana watenga matenda tsogolo lake liri pati? uli ndi mlandu kwa MULUNGU. GALU x 1000000

ken
ken
9 years ago

your coment is awaiting a moderation mmatathawuzanji? ndidzitukwana?

FKS
FKS
9 years ago

Iwe pa thako pa ana wayesa popangira gain pakopo patani? Panawonongeka ndiye ukufuna uwonongenso anawo eti? Its not too late usiye

Read previous post:
Malawi already preparing for post MDGs period

With the deadline for implementing the Millennium Development Goals (MDGs) coming next year, the Malawi government is already looking ahead,...

Close