Email a copy of 'Sex workers body date pub owners as prostitute claim police brutality' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Sex workers body date pub owners as prostitute claim police brutality' to a friend
Government has bowed down to the Judiciary support staff pay hike to accommodate house allowances. Judiciary support staff union spokesperson...
A HUMAN RIGHTS CHOONDE MTHANDIZENI MAYIYU APATSIDWE CHIPEPESO CHOYENERA. NO MATTER WHAT TYPE OF JOB SHE IS DOING DO NOT CONDEM HER, HUMAN RIGHTS IS HERE FOR ALL WITHOUT BIAS . NGATI MAYIYU SATHANDIZIDWA MABUNGWE A HUMAN RIGHTS ATSEKEDWE MZIKO MUNO ALEPHERA .. NTCHITO YANUTU NDI IMENEYI OSAMANGOLIMBANA NDI NDALE KUKAYENDA PANSEU.
IF YOU DO NOT ASSIST WE WILL ORGANISE A MARCH IN LILONGWE AND BLANTYRE AGAINST YOU PETITIONING TO THE RIGHT AUTHORITIES.
kodi bar iliyonse izichita kukhala ndi mahule ake odikilila panja??? zimenezi ayi. Azikazi athu sakumasuka tikapita nawo ku mowa. Mahulewa apeze mabanja. eeeeeee! ayi!
Mxiee!
Ife nkhani iliyonse ya uhule sitiyifuna. ameneyedwe ndithu mpaka azasiye. munthu wantundu wanji womadyela kumatako???????
Kwinanso kumakhala kupanda nzeru a polisiwo. For me already i see that the thug mentioned this woman to retaliate . the thug knew that the woman played a role in helping the police to arrest him. his mentioning of this woman is just to give her trouble. That should have been a consideration by the police. In any case they were supposed to question the woman but without brutality. Chonchi muzidabwa anthu akamaotcha ma police stations? ku polisi kwachuluka zitsiru zopanda nzeru
It was not fair kungoti a police adafa nzeru pang’ono .
Many have always said Malawi Police is full officers of beast in nature. Those who do not work for but against the people they are meant to protect and serve. This is particularly because of weak discipline measures within the Police that largely come due to currupted leadership at the highest level. Just imagine, today, the Police is headed by one who is linked to the murder of Robert Chasowa and the president is happy with that. This is the Police We have, Shame!
ZOCHITITSA MANYAZI NDI ZOMVETSA CHISONI KUTI MALO MOTI IFE NGATI MA HULE AGWIRE NAFE NTCHITO KUTI ADZIPEZA INFOR YOYENERA AKUTIZUZASO,APOLISI AMENEWO SITIWASIYA MPAKA ATALANDILA CHILANGO KUTI ASIYE ZOCHITSIRU ZAWOZO