Email a copy of 'Silver asks Sulom to dock Dwanga points for ‘fielding Mafco player’' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Silver asks Sulom to dock Dwanga points for ‘fielding Mafco player’' to a friend
The Nkukula Magistrate Court in Lilongwe on Monday convicted and fined three Malawians of Indians origin after they were found...
Kuzolowera kupeza mapoints aulere,koma pa ground kulephera.
mukufuna kupeza ma point aulele zauchitsiru basi palibe zimenezo ndipo a wliiam banda musalore zimenezo
To all football lovers, this claim by Silver is not true. am in the technical committee and we are too conversant with SULOM rules. DUFC is being run by well educated managers and we cant do such a thing. They never expected to drop points that’s why they have decided to do make such noise to buy sympathy
which techinical committee, silver, dwangwa, mafco or sulom??
Technical committee ya chani. kodi kudziikamo bwanji anthu inu. So you are saying fielding a player that is not eligible is ok just because you are in a technical committee of a team that you cannot mention. Go to hell
Ngati munagwiritsa ntchito player woti siwanu akuyenera kukulandani ma points. Silver yapanga ma draw eight ndipo iyiyi ndi ya nine bwanji pa ma game eight anapanga draw sanatulutsepo nkhani ngati imeneyi? Ngati Dwangwa siyolakwa ndekuti sailanda ma points koma ngati ili yolakwa ikuyenera kuluza ma points. Three seasons ago Silver inalandidwa three points ndikupereka kwa timu ya KB kamba koti Silver idagwiritsa ntchito player woti anali ndi ma yellow card awiri. Mu mpira muli malamulo ndipo malamulo amayenera kutsatidwa.