Email a copy of 'Sithole found guilty of cashgate; sentencing adjourned to Oct 28' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

60 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
Chifuniro zidana
Chifuniro zidana
9 years ago

Akhale dzaka 100 kut tikokere kumene anadyako mbava zazkulu ngat zmenez,agalu!

thabiso nkoana
thabiso nkoana
9 years ago

koma a polisi olembedwa ndi a mathanyula, manja m’thumba choncho koma akuperekeza mbava yayikulu ngati imeneyi. pa nyasaland amwene!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!

IAMATMYBESTWHENTHREATENED
IAMATMYBESTWHENTHREATENED
9 years ago

PP Thugs, can they expose the big fish too apa!! it is about time, she is busy jumping to other countries she better come and face the law!!

Gift Kaira
9 years ago

pi piiii !!!! odi uko amayi aduseko ndi wa chiwili wawo(zingayambe kuyiwalika) munya simunati

kamowa
9 years ago

wa Policeyo analembedwa ndi Peter.. mwaiwala kuti nthawi ya campagn ankangowatenga ndikuwalowesa ku PTS ku kanjedza

Jean Carrylani
9 years ago

Koma waPoliceyo zoona kupisira manja m’thumba choncho?…Akuti SWAGGA mwini wakeyo…Zili pa Nyasaland

Nyapala
9 years ago

At 26 and a house in area 47. Mwana anatasa ndi misonkho yathu uyu. Watsala Namata and Nantchito both mansion owners while most of us are strugglers. Area 6 where Maula Prison is located is waiting for you. Leonard Kalonga will have no chance for women and the title of Nyapala is waiting for you there together with Joster Njanji.

mayeso pindani
mayeso pindani
9 years ago

mpandeni wakubayo asala auntgate munya utsi mumadeweza kkkkkkkk

Imraan Sadick
9 years ago

10 years imprisonment with kalavula Deya would be befitting sentence for this youthful thief

Mbowe Mulambia
9 years ago

Malamulo a pa malawi ndi 0 pa hundred how come Lawyer Kasambara akuyimbidwa the same mulandu ali ndi ufuru oyimila anzake mulandu ofanana this is rabish these are thieves and Muhura is busy deffending mbava zoonekeratu ali mbava nayeso rotten country you need a wise to catch thieves osati tulo mulinato mu dziko muno changamukani a malawi.

Read previous post:
High Courts allows Lutepo access JB call logs

The High Court in Zomba has dismissed former President Joyce Banda's injunction stopping main cashgate suspect Osward Lutepo accessing her...

Close