Email a copy of 'Sulom dismisses Wanderers’ complaint over fixture congestion: Fear of match fixing in Malawi title' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Sulom dismisses Wanderers’ complaint over fixture congestion: Fear of match fixing in Malawi title' to a friend
Mzuzu City Council (MCC) chief executive officier Mcloud Kadam’manja has warned residents who are refusing to move out of disaster-prone...
Sulom ya Bullets chakuti chamanu nonse agalu inu
koma sulom zomwe ikupanga sizoona akufuna bullets itenge koma sizitheka ata league ndiya wandereres olo atapangana ndi satana wawo sizithekabe
Of coz even in the international leagues its only on the last day of the league that games start at the same time to avoid match fixing and stuff. But yeah until the last weeks of the league it would be hard for teams to play identical number of games. Especially with the situation where our teams dont have their own stadia that makes for a scheduling nightmare.
You are really a follower of football bro and you understand the game.
koma sulom chaka chino mwayesetsa kukhomelela mmmmmmmmmm tisaname.Komabe chomwe wakonza mulungu wina sangatsutsanenacho.Mudzafa ndiifa yowawa
Koma manoma tiyasamula zedi. No ball over the weekend.
lachinayi week yamawa nanga manoma ndiliti naweso
ATALEPHELA NTCHITO YAWO POGAMULA MOKHOMELERA WANDERERS, AKA NDI KACHIKENANSO KUYIKHOMELELA KUTI WANDERERS IDZISEWELA ILI UNDER PREASURE KOMABE IFEYO MONGA MANOMA LEAGUE TITENGA NDITHU KUTI AGALU A SULOM ACHITE MANYAZI, APHYE MTIMA MPAKA AKODZE MAGAZI. MANOMAAAHHH, WE’RE AL FORWARD WITH BE FORWARD
Sulom ya Bata, tiwinabe mukhaula
kunjenjemera bwanji? kulilira zomwezi?
Yankho Yapuwa, u r a soccer fan who knows the realities osati bwebwebwe bwebwebwe bola naonso apanga post. Anakuuzani ndani kuti Sulom izabakira NOMADS pa zinthu zopanda mchere. Ngati League mwaifuna, winani pa ground osati pakamwa, koma mziwenso kuti Mzuni ikuchinyanibee.