Email a copy of 'Sulom intervenes in Wanderers ‘coup’: Sponsors Be Forward ‘monitoring the situation’' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

22 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
Alex Tulamah Tulamah
8 years ago

Inu mukufuna team ya fuko la anthu odzikirai ikhale ya masiye ngati zaka zingapo zapitazi iiiii a Malawi mwatani kodi ndalama zomwe mukulimbirana zake aaaaa bola ndizigwira ganyu yokumba zimbudzi za wanthu than tindalama tomwe mukulimbirana zakezo umbuli basi isiyeni team basi yokha.Nditsireni NOMA YANGAI AKUBA INU

Beston
Beston
8 years ago

I will keep on supporting noma no matter what

Patrick
8 years ago

I am Matemba junior,I assume wanderes still need to use the same strategies that my father used when wanderes was the most successful team in Malawi.

madzi
8 years ago

naga player no 12 alikiti ..Wter …Lero dzakunyelani bakha inu…noooma, zopusa.

Wanganya
Wanganya
8 years ago

Abb ambuli samadziwa asiyen this is why malawi zinthu sizayenda mpaka kale kale Chifukwa chake mchimenecho taluza kangati a bb ali momo? Osamachita manyaz ponena bwa? Wa police wa ku nsanje akatumizidwa Kunja amati malawi Kapena wa ku nsanje? Umbuli bwanji ?

Mzungu Malawiano
Mzungu Malawiano
8 years ago

Money does not buy success. To some money even chokes hardwork.

short wamtali
short wamtali
8 years ago

A UNECA palibe nkhani apa anthuwo akamati bb2 inayo 1 akungonyadira maplayers awo koma chenicheni akuchiziwa mpira ndi anthu 11 mu ground. Popeza mpira ndizigoli ndichifukwa ogoletsa amatchuka kuposa Ena onse. BB woyee! Chiukepo woyee! Sailesi woyee! Inenso woyee! Yakugogodani pachifuwa neighbor imeneyi?

wayunda
8 years ago

A coach ndi executive panel yanu musangowonerela team yikufowoka ayi.osamakhala ndi maganizo oti malingana za ine zikuyenda

mphatso
mphatso
8 years ago

wanderers people please sort yourselves out as soon as possible for the betterment of the game.We don’t want this kind of rubbish in our soccer.You are always chasing sponsors because of umbuli.kodi team simaluza?look at teams in Europe and elsewhere teams like arsenal you wont hear this kind of rubbish…

pido
8 years ago

Ndalama zavuta Ma supporters in Malawi sadziwa chomwe akupanga. Awa a Chiwambo kusokosera kwambiri osadziwa kuti naonso akuononga. Zopusa basi

Read previous post:
Activist Mfiti says oil exploration in Lake Malawi must be stopped

A local environmental activist Godfrey Mfiti is persuading government to cancel oil exploration in Lake Malawi, saying it is categorised...

Close