Email a copy of 'Super League of Malawi top brass to run in polls ' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Super League of Malawi top brass to run in polls ' to a friend
Chinese national Chain Weging, 41, has been arrested in Malawi’s capital Lilongwe for counterfeiting wool products from Sakiza Spinning...
Bottoman Woyeee, Your Committee was not Biase no Team was above the law,
This rotten Solom should pack and go.Azikakhala ku ma open stand basi.Yatha nthawi yanu.
Mmesa mudaphetsa munthu osalakwa ku Balaka ndiye mufuna kuimaso agaru inu. Fakiyuuuuuuu.
Kunena mosabisa Mr Botomani, William Banda and the rest of SULOM alephera kuyendetsa ligi makamaka yangothayi. Ine ndikudabwa anthu akamanena kuti season yangothayi yayenda bwino. Munamvapo kuti ligi komwe timu imapezeka ikusewera round yathunthu ya season ma away games okhaokha kapena magemu onse kukhala apakhomo? Nde zinthu zikatero tidziti ligi yathu ikuyenda bwino? So laughable.
Again, SULOM yalephera kupanga treat matimu onse amu ligi fairly makamaka when it comes to meting out punishments. Matimu ena kulandira chilango amalandira chachikulu komanso sipamapita nthawi yayitali pamene ena kumakhala kaye kuzengeleza.
MWACHIDULE – Botomani, Williams Banda and the rest adzipita basi.
Super League of Malawi is da worst-run league in the world!
Akulu tapezani zochita zenizeni nanga zimenezi zikuthandizani? Mufuna muzingotimvuta ndi pasamvute wanuyo? cholinga silver isatengenso super legue? mwalephera a Botomani simudzawina.